1. Mukangodzuka, pukutani nkhope yanu ndi m’maso pogwiritsa ntchito manja anu onse kuti muchotse chitulotulo. 2. Mukadzuka, werengani mawu awa: الْحَمْدُ للَّه الَّذِي أَحْيَانَا بَعْدَ مَا أَمَاتَنَا وَإِلَيْهِ النُّشُورُ Kutamandidwa konse ndi kwa Allah yemwe watipatsa moyo pambuyo pa imfa ndipo kwa iye ndikobwelera. 3. Mukadzuka, tsukani mkamwa ndi miswaak. …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu