Mmahadith ambiri, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) adauchenjeza Ummah za Dajjaal ndi mayesero ndi masautso omwe Asilamu adzakumane nawo akadzatulukira padziko lapansi. Momwemonso, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) adafotokoza momveka bwino momwe Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) ndi Asilamu adzamenyanirane naye pankhondo, ndi momwe Nabiy Isa …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu