Daily Archives: November 14, 2026

Sunnat Ndi Aadaab Za Pa Ulendo 1

1. Munthu asanapite paulendo (ngati ulendo opita kutali ntunda okwana makilomita 78 kapena kuposerapo), ayenera kuswali ma rakah awiri a salaah. Salaah iyi imadziwika kuti Salaatus Safar. Mut’im bun Miqdaam rahimahullah adati Mtumiki Swallallahu alaihi wasallam adati: “Palibe ntchito imene munthu angasiire banja lake asananyamuke paulendo wabwino kwambiri kuposa ma …

Read More »