Werenga mdzina la mbuye wako yemwe adalenga (chinachirichonse), adamulenga munthu kuchokera ku dontho la magazi, ndipo mbuye wako ndi olemekezeka, amene adamuphunzitsa munthu kulemba (pogwiritsa ntchito) cholembera, adamuphunzitsa munthu zinthu zomwe zankazidziwa, kotero munthu wapsyola malire chifukwa akudzitenga kuti iye atha kudziimira payekha, ndithudi, kwa mbuye wanu ndiye kobwelera, kodi wamuona uyo (Abu Jahal) amene akuletsa kapolo (Muhammad sallallahu alaih wasallam) akaima kuti apemphere, tandiuza kodi ngati iyeyo (kapolo wanga - Muhammad (sallallah alaih wasallam) ali pa chiongoko kapena akuwalamulira anthu kuchita ntchito zabwino nankha Abu Jahal ali ndi mphamvu zanji kuti amuletse)? Tandiuza ngati iyeyo (Abu Jahal) angakane ndikubwelera m'mbuyo, kodi sakuzindikira kuti Allah Ta’ala akuona zomwe oye akuchhitazo? Sichoncho, ngati sasiya zomwe akuchitazo timukoka tsitsi la paliombo (tiligwira mwamphanvu liombi lake ndikukamponya kumoto. Basi, ayitane gulu lakero ifenso tiitana asilikali athu a kumoto, sichoncho, usamunvere ameneyo oh Muhammad (sallallahu alaih wasallam) (pazimene akukuletsazo, ndipo gwetsa nkhope yako pansi ndipo udziyandikitse kwa mbuye wako.
Read More »Kuthandizidwa pa Mlatho wa Siraat
عن عبد الرحمن بن سمرة قال: خرج رسول الله صلى الله عليه وسلم فقال: إني رأيت البارحة عجبا … ورأيت رجلا من أمتي يزحف على الصراط مرة ويجثو مرة ويتعلق مرة فجاءته صلاته علي فأخذت بيده فأقامته على الصراط حتى جاوز ورأيت رجلا من أمتي انتهى إلى أبواب الجنة فغلقت …
Read More »Duwa Kutha Kwa Azaana
2. Mukatsiriza kuwerenga duwa kutha kwa adhaana duwa iyinso mukuyenera kuwerengedwa. أَشْهَدُ أَنْ لَّا إِلٰهَ إِلَّا اللهُ وَحْدَهُ لَا شَرِيْكَ لَهُ وَأَنَّ مُحَمَّدًا عَبْدُهُ وَرَسُوْلُهُ رَضِيْتُ بِاللهِ رَبًّا وَبِمُحَمَّدٍ رَسُوْلًا وَبِالْإِسْلَامِ دِيْنًا Ndikuchitira Umboni kuti kulibe wina opembedzedwa mwachoonadi koma Allah yekha, Iye ndimmodzi yekha ndipo alibe ophatikizana naye. Ndiponso …
Read More »Kuteteza Dua ya Mtumiki (sallallahu alaih wasallam)
عن أنس بن مالك قال:قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: من صلى علي بلغتني صلاته وصليت عليه وكتبت له سوى ذلك عشر حسنات (المعجم الأوسط للطبراني، وسنده لا بأس به كما القول البديع صـ 239) Olemekezeka Anas (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adayankhula kuti: munthu amene …
Read More »Duwa Kutha Kwa Azaana
1. Ikatha Adhaan mukuyenera kuwerenga duruud pomufunira zabwino Mtumiki (sallallah alayhi wasallam).Pambuyo pake nenani duwa iyi:[1] اَللّٰهُمَّ رَبَّ هٰذِهِ الدَّعْوَةِ التَّامَّةِ وَالصَّلَاةِ الْقَائِمَةِ آتِ مُحَمَّدًانِ الْوَسِيْلَةَ وَالْفَضِيْلَةَ وَابْعَثْهُ مَقَامًا مَّحْمُوْدًانِ الَّذِيْ وَعَدْتَّهُ إِنَّكَ لَاتُخْلِفُ الْمِيْعَادْ Oh Allah, Ndiinu Mbuye (mwini) wakuitana uku kwabwino kokwanilira ndiponso kuswala yomwe ili yopitilira. Mpatseni …
Read More »Njira yodziyetsera ku machimo
عن أبي هريرة رضي الله عنه قال : قال رسول الله صلى الله عليه وسلم : أكثروا الصلاة علي في الليلة الزهراء واليوم الأغر فإن صلاتكم تعرض علي (المعجم الاوسط للطبراني وسنده ضعيف لكن يتقوى بشواهده كما في القول البديع صـ 325) Sayyiduna Abu Hurairah radhiyallahu anhu akufotokoza kuti Mtumiki …
Read More »Kuyankha Adhaan
Adhaan ndichizindikiro chachikulu chachisilamu. chifukwa choti adhaana ndichizindikiro chachikulu pachipembedzo chachisilamu tikuyenera kuonetsera ulemu ku adhaana ikamapangidwa poyankha, komanso ikamapangidwa osakhala otangwanika ndizinthu zamdziko lapansi. Ndipo sizofunikira pamene adhaana ikuchitika munthu kukhala otangwanika ndikuyankhula zinthu zamdziko lapansi.[1] 1) Pamene ikupangidwa adhaana, yankhani potsatizira mawu amene muadhini (opanga adhaana) akunena.[2] mwachitsanzo …
Read More »Tafseer Ya Surah Teen
وَالتِّينِ وَالزَّيْتُونِ ﴿١﴾ وَطُورِ سِينِينَ ﴿٢﴾ وَهَـٰذَا الْبَلَدِ الْأَمِينِ ﴿٣﴾ لَقَدْ خَلَقْنَا الْإِنسَانَ فِي أَحْسَنِ تَقْوِيمٍ ﴿٤﴾ ثُمَّ رَدَدْنَاهُ أَسْفَلَ سَافِلِينَ ﴿٥﴾ إِلَّا الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ فَلَهُمْ أَجْرٌ غَيْرُ مَمْنُونٍ ﴿٦﴾ فَمَا يُكَذِّبُكَ بَعْدُ بِالدِّينِ ﴿٧﴾ أَلَيْسَ اللّٰـهُ بِاَحْكَمِ الْحَاكِمِينَ ﴿٨﴾ Ndikulumbilira mitengo ya Mkuyu ndi Zitona, ndikulumbiliranso phiri la Sinai, …
Read More »Kapangidwe Ka Adhaan Ya Fajr/Subuhi
Ngati wina akupanga Adhaan ya fajr adzapanga monga zalongosoleredwera m’mbuyomu. kusiyana kudzangokhala koti akadzamaliza kunena mawu oti حي على الفلاح adzanena mawu:[1] اَلصَّلَاةُ خَيْرٌ مِّنَ النَّوْمْ Swalah ndi yabwino kuposa tulo. عن محمد بن عبد الملك بن أبي محذورة عن أبيه عن جده رضي الله عنه قال قلت يا رسول …
Read More »Kupeza Sawabu Zokwana Qeeraat Imodzi
عن علي بن أبي طالب رضي الله عنه أن رسول الله صلى الله عليه وسلم قال : من صلى علي صلاة كتب الله له قيراطا والقيراط مثل أحد (مصنف عبد الرزاق، الرقم: 153، وسنده ضعيف كما في القول البديع صـ 260) Sayyiduna Aliy bin Abi Taalib radhiyallahu anhu akufotokoza kuti …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu