Kutonthoza Oferedwa

Kutonthoza Oferedwa

13. Sizoloredwa kupita ku nyumba ya kafiri yemwe wamwalira kukapepesa mwambo wamaliro uli mkati. Koma akakhala kuti ndi kafiri oyandikana naye nyumba kapena kaafir aliyense amene wataya wachibale wake, mwachitsanzo, mwana, ukhoza kumutonthoza ndi mawu awa: أَخْلَفَ اللّه عَلَيْكَ خَيْرًا مِنْهُوَاَصْلَحَكَ Akhlafa Allahu ‘Alayka Khayran Minhu Wa ‘Aslahaka Allah akupatse …

Read More »

Kutonthoza Oferedwa

7. Nkoloredwa kuyamikira omwalirayo. Komabe, pomutamanda, onetsetsani kuti simukukokomeza kapena kumutamanda pa makharidwe amene panalibe mwa iye. Momwemonso musatengere chikharidwe ndi njira za makafiri pomutamanda. 8. kuchuluka kwa nthawi ya ta’ziyat ndi masiku atatu kuchokera tsiku lomwalira. Pambuyo pa tsiku lachitatu, ndi makruh kupanga ta’ziyat. Komabe, ngati munthu sadathe kubwera …

Read More »

Ma Sunnah Komanso Miyambo Yochezera Ndi Namfedwa

1. Ta’ziat imatanthauza kugawana chisoni ndi ananfedwa ndi kuwamvera chisoni pa kutaika kwa okondedwa wawo. Izi zimachitika pomupangira dua omwalirayo pamaso pa akubanja ake. Momwemonso izi zidzachitika polipangira Dua banja lake, kupempha Allah Odalitsika ndi Wapamwambamwamba, kuti awadalitse powapatsa kupilira ku mayesero amenewa. 2. Dua ingachitike m’mawu awa: “Allah amupatse …

Read More »

Kutonthoza Oferedwa

Chisilamu ndi njira yokwanira komanso yangwiro ya moyo yomwe yaganizira zosowa zonse za munthu. Sizinangosonyeza njira ya mtendere m’moyo wa munthu, komanso zasonyeza mmene tingasonyezere chikondi ndi mtendere munthu akamwalira. Choncho Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adausonyezera Ummah momwe ungatonthozere ndi kuwapepesa ofedwa amene ali m’masautso. Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adati: …

Read More »