Kudzuka

Madua Omwe Ndi Sunnah Kuwerenga Pa Swalah Ya Tahajjud

Mukaiyamba Swala ya Tahajjud, werengani ma dua awa musanawerenge Surah Faatihah: Dua One اَللّٰهُمَّ لَكَ الْحَمْدُ أَنْتَ قَيِّمُ السَّمٰوَاتِ وَالْأَرْضِ وَمَنْ فِيْهِنَّ وَلَكَ الْحَمْدُ لَكَ مُلْكُ السَّمٰوَاتِ وَالْأَرْضِ وَمَنْ فِيْهِنَّ وَلَكَ الْحَمْدُ اَنْتَ نُوْرُ السَّمٰوَاتِ وَالْأَرْضِ وَمَنْ فِيْهِنَّ وَلَكَ الْحَمْدُ أَنْتَ الْحَقُّ وَوَعْدُكَ الْحَقُّ وَلِقَاؤُكَ حَقٌّ وَقَوْلُكَ حَقٌّ وَالْجَنَّةُ حَقٌّ …

Read More »

Ma Dua Omwe Ndi Sunnah Kuwerenga Podzuka

Dua 1 الْحَمْدُ لِلَّهِ الَّذِي أَحْيَانَا بَعْدَ مَا أَمَاتَنَا وَإِلَيْهِ النُّشُورُ Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu Talaa yemwe adatipatsa moyo pambuyo pa imfa ndipo kwa lye yekha ndi kumene tidzabwerere. Dua 2 الْحَمْدُ لِلَّهِ الَّذِي عَافَانِي فِي جَسَدِي وَرَدَّ عَلَيَّ رُوْحِيْ وَأَذِنَ لِي بِذِكْرِهِ Kuyamikidwa konse ndi kwa Allah Talaa …

Read More »

Sunnats Ndi Aadaab Za Podzuka

1. Mukangodzuka, pukutani nkhope yanu ndi m’maso pogwiritsa ntchito manja anu onse kuti muchotse chitulotulo. 2. Mukadzuka, werengani mawu awa: الْحَمْدُ للَّه الَّذِي أَحْيَانَا بَعْدَ مَا أَمَاتَنَا وَإِلَيْهِ النُّشُورُ Kutamandidwa konse ndi kwa Allah yemwe watipatsa moyo pambuyo pa imfa ndipo kwa iye ndikobwelera. 3. Mukadzuka, tsukani mkamwa ndi miswaak. …

Read More »

Kudzuka

Tisanagone, taphunzitsidwa kubwereza madua a masnoon ndikumutchura Allah. Mwa ma dua a masnoon tisanagone, pali dua iyi: اللَّهُمَّ بِاسْمِكَ أَمُوْتُ وَأَحْيٰى O Allah Ta’ala ndi dzina lanu, ndikufa ndikukhala ndi moyo. Mu dua iyi, tulo lafaniziridwa ndi imfa, chifukwa chakuti munthu akagona, samakhalanso ndi mphamvu komanso kuzindikira zomwe zikuchitika. Choncho, …

Read More »