6. Iwerengeninso dua iyi pamene muli Pa Jalsah:[1] اللَّهُمَّ اغْفِرْ لِي، وَارْحَمْنِي، وَعَافِنِي، وَاجْبُرْنِي، وَارْفَعْنِي، وَاهْدِنِي، وَارْزُقْنِي Oh Allah, ndikhululukireni, ndichitireni chifundo, ndichotsereni kufooka kwanga, ndikwezeni pa udindo, ndiongolereni ndi kundidalitsa ndi riziki. 7. Nenani takbira ndipo pitirirani ku sajda yachiwiri monga mwachizolowezi.[2] 8. Imirirani kuchokera pa sajdah yachiwiri nkukhala …
Read More »Monthly Archives: February 2023
Hazrat Abu Bakr – manthu cha Ubwino ndi Chifundo
Tsiku lina Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adafunsa kwa ma Swahaabah (radhwiyallahu “anhum) kuti: “Ndani mwa inu amene akusala kudya lero?” Hazrat Abu Bakr (radhiyallahu anhu) adayankha: “Lero ndasala. Kenako Nabiy (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adafunsa. “Ndani mwa inu amene wayendera munthu wodwala lero?” Harrat Abu Bakr (radhiyallahu ‘anhu) adayankha: “Lero ndayendera …
Read More »Sajdah
12. Werengani Takbiir ndikukhala pansi mukachoka pa Sajdah yoyamba, imeneyi imatchedwa kuti I’tidaal.[1] Jalsah 1. Mukukhala kwanu pa jalsah, ikani manja anu pa ntchafu zanu ndi zala zanu pafupi ndi mawondo anu.[2] 2. Gwirizanitsani zala zanu.[3] 3. Yang’anani malo a Sajdah uku muli pa Jalsah.[4] 4. Phazi lakumanja likhale lolunjika …
Read More »Munthu Woyamba wa Ummah uwu kukalowa ku Jannah
M’ Hadith ya yodaliysika, Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adalongosora kuti Ummah wake udzalowa ku Jannah pamaso pa ma Ummah ena onse, ndipo kuchokera mu Ummah wake wonse, Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adzakhala munthu woyamba kulowa ku Jannah pambuyo pake. Mtumiki (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adati: “Hazrat Jibreel (‘alaihis salaam) adaonekera …
Read More »Ubwino Waukulu Wowerenga Durood Tsiku la Jumuah
عن أوس بن أوس قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: إن من أفضل أيامكم يوم الجمعة فيه خلق آدم وفيه قبض وفيه النفخة وفيه الصعقة فأكثروا علي من الصلاة فيه فإن صلاتكم معروضة علي قال: قالوا: يا رسول الله وكيف تعرض صلاتنا عليك وقد أرمت يقولون بليت فقال: …
Read More »Sajdah
7. Asungeni manja anu M’mbali.[1] 8. Yang’anani pa malo a Sajdah.[2] 9. Sungani mpata pakati pa mimba ndi ntchafu.[3] 10. Miyendo yonse iwiri ikhale pansi ndi zala zammiyendo zitaloza ku chibla. Sungani mpata wa dzanja limodzi pakati pa mapazi anu pa sajdah.[4] 11. Werengani katatu kapena nambala yosagawika ndi 2 …
Read More »Hazrat Abu Bakr (Radhwiyallahu ‘anhu) akhala Wokonzeka kupereka nsembe ya china Chilichonse
Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wa sallam) Pankhondo ya Badr, mwana wa Abu Bakr Siddeeq (radhwiyallahu anhu) Hazrat Abdur Rahmaan (Radhwiyallahu ‘anhu), anamenya nawo mbali ya okanira poti iye adali asadakhulupirirebe Chisilamu. Pambuyo pake, atalowa Chisilamu, ali chikhalire pansi ndi bambo ake, Hazrat Abu Bakr Siddeeq (Radhwiyallahu “anhu), adati: “E, inu abambo …
Read More »Tafseer Ya Surah Kaafiroon
بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ يَا أَيُّهَا الْكَافِرُونَ ﴿١﴾ لَا أَعْبُدُ مَا تَعْبُدُونَ ﴿٢﴾ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ﴿٣﴾ وَلَا أَنَا عَابِدٌ مَّا عَبَدتُّمْ ﴿٤﴾ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ﴿٥﴾ لَكُمْ دِينُكُمْ وَلِيَ دِينِ ﴿٦﴾ Nena: “E, inu anthu osakhulupirira! Ine sindingapembedze (mafano) amene mukuwapembedza, ndiponso simum’pembedza Amene ine ndikum’pembedza (Allah Ta’ala). Ndipo inu simunhampembedze (Allah) Amene ine ndikumupembedza …
Read More »Sajdah
1. Nenani takbira, ndipo popanda kukweza manja anu, pitani pa sajdah.[1] 2. Gwirani manja m’maondo uku mukupita pa Sajdah.[2] 3. Yambani ndikuika mawondo pansi, kenako manja, ndipo pomalizira pake Ikani chipumi ndi mphuno pamodzi.[3] 4. Ikani zikhatho pansi m’njira yoti zala zifanane ndi makutu ndipo mbali zapansi zigwirizane ndi mapewa.[4] …
Read More »Chikondi cha Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) Kugwirizana ndi Chikondi cha Rasulullah (Sallallahu ‘alaihi wasallam)
Bambo ake a Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) atalowa Chisilamu. Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adalankhula kwa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) kuti: “Ndikulumbirira amene anakuikani m’choonadi! Ngakhale ndiri mchisangalaro kuti bambo anga alowa chisilamu, ndikadakhala osangalala kwambiri zikanakhala kuti omwe alowa chisilamu ndi amalume anu Abu …
Read More »