Daily Archives: December 16, 2024

Kulandira dzina la Al-Fayyadh kuchokera kwa Mtumiki swallallahu alaihi wasallam

Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) adampatsa olemekezeka Talhah (radhwiyallahu ‘anhu) dzina loti Al-Fayyaadh (munthu owolowa manja kwambiri) kangapo. Pansipa pali nkhani imodzi yotere: Pankhondo ya Zi Qarad, Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) adadutsa pachitsime cha Baisaan. Madzi a m’chitsimechi ankadziwika kuti ndi anchere. Rasulullah (Swalla Allaahu …

Read More »