1. Ndi mustahab (zofunika kwambiri) kupanga wudhu usanakamuyendere odwala.[1] Olemekezeka Anas Radhwiyallahu anhu akusimba kuti Rasulullah swallallahu alaihi wasallam adati; “Amene wapanga wudhu wangwiro (pokwaniritsa masunnah ndi ma mustahab onse a wudhu) ndi kupita kukacheza ndi m’bale wake wachisilamu yemwe akudwala ndi chiyembekezo cholandira malipiro oyendera odwala, munthu oteroyo adzaikidwa …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu