Dua Yoyamba لا يَأْسَ طَهُورٌ إِنْ شَاءَ الله Palibe chifukwa chodera nkhawa, insha-Allah kudzera m’matendawa, muyeretsedwa. (i.e. Palibenso chifukwa chilichonse choti mude nkhawa kapena kuchita mantha. Mukungoyeretsedwa ku Uzimu, mukuyeretsedwa ku machimo anu, ndipo kuthupi, thupi lanu likuyeretsedwa ku poizoni. Choncho, pamene matenda abwera kwa inu ngati chifundo chobisika kumbali …
Read More »Ma Sunnah Komanso Miyambo Yokaonera Odwala 2
4. Mukamayendera odwala, pemphani dua iyi: لا بَأْسَ طَهُورٌ إِنْ شَاءَ اللهُ Palibe chifukwa chodera nkhawa, insha-Allah kudzera mu matendawa, muyeretsedwa. Mukhozanso kubwereza dua iyi kasanu ndi kawiri: أَسْأَلُ اللهَ الْعَظِيمَ رَبَّ الْعَرْشِ الْعَظِيمِ أَنْ يُشْفِيكَ Ndikumupempha Allah Wamphamvu zoposa, Mbuye wa Mpando Wachifumu waukulu, kuti akuchizeni. عن ابن عباس …
Read More »Ma Sunnah Komanso Miyambo Yokaonera Odwala
1. Ndi mustahab (zofunika kwambiri) kupanga wudhu usanakamuyendere odwala.[1] Olemekezeka Anas Radhwiyallahu anhu akusimba kuti Rasulullah swallallahu alaihi wasallam adati; “Amene wapanga wudhu wangwiro (pokwaniritsa masunnah ndi ma mustahab onse a wudhu) ndi kupita kukacheza ndi m’bale wake wachisilamu yemwe akudwala ndi chiyembekezo cholandira malipiro oyendera odwala, munthu oteroyo adzaikidwa …
Read More »Ubwino Oyendera Odwala 2
Kutalikitsidwa ndi Jahannam kwa ntunda okwana kuyenda zaka makumi asanu ndi awiri (70) Olemekezeka Anas (Radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) adati: “Amene wapanga wudhu olongosoka (pokwaniritsa masunnah ndi ma mustahabbaat) ndi kupita kukamuona m’silamu nzake yemwe akudwala ndi chiyembekezo choti adzalandire malipiro okayendera nsilamu odwala, munthu oteroyo …
Read More »Ubwino Oyendera Odwala 1
Kupeza Mwayi Opangiridwa Dua Ndi Angelo Okwana Zikwi Makumi Asanu Ndi Awiri (70,000) Olemekezeka Ali (Radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) adati: “Amene amayendera odwala m’bandakucha, angero zikwi makumi asanu ndi awiri (70,000) amamupemphera chifundo kwa Allah mpaka madzulo; Amene angamuyendere odwala madzulo angelo okwana 70,000 amamupemphera chifundo …
Read More »Kuyendera Odwala
Chipembedzo cha Chisilamu chimalimbikitsa ndi kulamula kuti munthu akwaniritse udindo umene ali nawo kwa Allah ndi udindo umene ali nawo kwa akapolo a Allah. Pankhani ya udindo ndi maufulu omwe munthu ali nawo pa akapolo a Allah, izi zikhoza kugawidwa m’mitundu iwiri ya maufulu. Mtundu oyamba ndi ufulu umene uli …
Read More »