Kukhululukidwa Kwa Machimo kudzera mukuswali Jumuah Abu Hurairah (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) adati: “Machimo omwe achitika pakati pa Jumu’ah ziwiri, ngati sali machimo akuluakulu, Allah amakhululuka. Tsiku Lopatulika kwa Okhulupirira Ibnu Abbaas (radhwiyallahu anhuma) adanena kuti Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) adati: “Tsiku ili (tsiku la Jumu’ah) …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu