́Allaamah Zurqaani (Rahimahullah) wapereka nkhani iyi kuchokera kwa Haafiz ibn ‘Asaakir (rahimahullah) ndi mndandanda wamphamvu wa osimba nkhani: Atamwalira Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam), zinali zovuta kwa olemekezeka Bilaal (radhwiyallahu ‘anhu) kupitiriza kukhala ku Madinah Munawwarah cha okondeka wake kwambiri Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) ndi …
Read More »Monthly Archives: October 2025
Ubwino wa Jumuah
Kukhululukidwa Kwa Machimo kudzera mukuswali Jumuah Abu Hurairah (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) adati: “Machimo omwe achitika pakati pa Jumu’ah ziwiri, ngati sali machimo akuluakulu, Allah amakhululuka. Tsiku Lopatulika kwa Okhulupirira Ibnu Abbaas (radhwiyallahu anhuma) adanena kuti Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) adati: “Tsiku ili (tsiku la Jumu’ah) …
Read More »Dua ya Bilaal (Radhwiyallahu ‘anhu) kuwapemphera chiongoko ma Quraish.
Olemekezeka ‘Urwah bun Zubair (rahimahullah) anasimba kuti mkazi wina wa m’banja la Banu Najjaar (yemwe ndi Nawwaar bint Maalik, mayi ake a Zaid bin Thaabit (radhwiyallahu ‘anhuma)) adati: “Nyumba yanga inali pamalo okwera ndipo inali imodzi mwa nyumba zapamwamba za Mus. “Bilaal (Radhwiya Allaahu ‘anhu) ankaitana azaan ya Fajr kuchokera …
Read More »Jumuah
Tsiku la Jumu’ah ndi lofunikira kwambiri mu Chisilamu. Izi ndi zina mwa zabwino zazikulu za Allah pa Ummah uwu ndipo ndichinthu chodziwika bwino m’Chisilamu. Rasulullah (sallallahu ‘alaihi wasallam) adati: “Tsiku la Jumu’ah ndi sayyidul ayyaam (lomwe ndi mtsogoleri wa masiku onse), ndi tsiku lalikulu kwambiri (kuchokera m’masiku a msabata) pamaso …
Read More »Olemekezeka Bilaal (Radhwiya Allaahu ‘anhu) Ayang’anira ndi Kusunga Mkondo wa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam)
Mfumu yaku Abysinia (Najaashi (rahimahullah)) nthawi ina inatumiza mikondo itatu kwa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) ngati mphatso. Atalandira mikondo itatu ija, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) adapereka mkondo umodzi kwa Ali (radhwiyallahu ‘anhu), adapereka mkondo wachiwiri kwa Umar (Radhwiyallahu ‘anhu) ndipo adadzisungira yekha …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu