Imaam Bayhaqi (rahimahullah) akunena kuti: Yazid bin Abi Sufyaan (radhiyallahu ‘anhu) pamene adali bwanamkubwa wa Shaam, Asilamu adachita Jihaad ndipo adapambana, motero adapeza chuma cholanda kwa adani. Mkatikati mwa katundu ameneyo mudalinso mtsikana okongola yemwe adaperekedwa kwa msilikali wina wachisilamu ngati gawo lake. Msilikaliyu atangolandira gawo lakeli (mtsikananayu), Yazid bin …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu