Ma Sunnah Ena Onse ndi Aadaab Okhudzana ndi Kudya 1. Musachidandaule kapena kuchipezera vuto chakudya. Olemekezeka Abu Hurairah radhwiyallahu anhu akunena kuti Rasulullah swallallah alaihi wasallam sanachipezereko vuto chakudya. Ngati akufuna kudya ankadya, ndipo ngati sanachifune ankachisiya (popanda kuchipezera vuto). 2. Musadye chakudya chotentha kwambiri. Olemekezeka Asmaa bint Abi Bakr …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu