Monthly Archives: April 2026

Kulimba Mtima kwa Hazrat Abdullah bin Mas’uud (Radhiyallahu ‘anhu)

Pankhondo ya Hunain, Asilamu adagonjetsedwa kwakanthawi kochepa. Munthawi yovutayi, Hazrat Abdullah bin Mas’uud (Radhwiyallahu ‘anhu) adali m’gulu la ma swahaabah (Radhwiyallahu ‘anhum) amene adapirirabe ndikukhala limodzi Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam). Hazrat Abdullah bin Mas’ood (radhwiyallahu ‘anhu) akufotokoza kuti: “Ndinali ndi Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) tsiku la …

Read More »

Ma Dua Onena Ukamaliza Kudya

Dua Yoyamba اَلْحَمْدُ لِله الَّذِي أَطْعَمَنَا وَسَقَانَا وَجَعَلَنَا مُسْلِمِينَ Kuyamikidwa konse ndi kwa Allah amene watipatsa chakudya ndi chakumwa ndi kutipanga kukhala Asilamu. Dua Yachiwiri الْحَمْدُ لِلَّهِ الَّذِي أَطْعَمَنِيْ هَذَا الطَّعَامَ وَرَزَقَنِيْهِ مِنْ غَيْرِ حَوْلٍ مِّنّّي وَلاَ قُوَّةٍ Kuyamikidwa konse ndi kwa Allah amene wandipatsa chakudya ichi kuti ndidye, ndipo …

Read More »