Mtumiki (swallallahu ‘alaihi wasallam) anatumiza Mu’aaz (radhwiyallahu ‘anhu) kuti akalamulire gawo lina la Yemen, ndipo Abu Musa Ash’ari (radhwiyalllahu ‘anhu) akalamulire gawo lina. Mtumiki (swallallahu ‘alaihi wasallam) anawalankhula ndipo anawapatsa uphungu otsatirawu asanawatumize. Anawauza kuti, “Fewetsani zinthu (kwa anthu), ndipo musawakhwimitsire. Perekani uthenga wabwino (kwa anthu), ndipo musawathamangitse (ku dini).” …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu