Daily Archives: October 19, 2026

Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) Osafuna Kuchitidwa Opaleshoni ya Diso Chifukwa Chopereka Vuto ku Swalah Yake

Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) adadwala diso zomwe zidapangitsa kuti lidzitulutsa madzi nthawi zonse. Dokotala adamulangiza kuti, “Ndizotheka kuthana nalo vutolo ngati ukufuna kutenga njira zodzitetezera pochita sajdah pa thabwa kwa masiku asanu, osati pansi.” Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) anayankha kuti, “Sindiri okonzeka kuchita zimenezo. Sindingaswali ngakhale rakah imodzi …

Read More »