Daily Archives: October 27, 2026

Kusamala pa Gwero la Munthu Wopeza Chidziwitso cha Deeni

  Nthawi ina munthu wina dzina lake Bushair bin Ka’b al-Adawi adadzakumana ndi Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma). Adayamba kuyankhulana, ndipo mkati mwa zokambiranazo, Bushair adafotokoza Mahadeeth a Rasulullah (Swalla llahu alaihi wasallam) kwa Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma). Abdullah bun Abbaas (Radhwiyallahu ‘anhuma) sadaonetse chidwi chilichonse pa mahadith ena …

Read More »