Nthawi ina, Abu Hurairah (radhwiyallahu ‘anhu) adawayankhula anthu nati: Anthu inu mukunena kuti, “Bwanji Abu Hurairah akufotokoza Mahaadith ambiri kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam), pomwe ma Swahaabah ena ngati ma Muhaajireen ndi Ansaaar sakunena mahaadith ochuluka choncho kuchokera kwa Rasulullah (Swallallahu ‘alaihi wasallam)?” Chifukwa chake n’chakuti nthawi …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu