Kuopa Allah Taala

Qataadah (Rahimahullah) akusimba kuti Olemekezeka Abu Ubaidah (Radhwiyallahu ‘anhu) ankati, (chifukwa choopa kudzaima pamaso pa Allah Ta’ala pa tsiku la Qiyamah ndi kuwerengetsedwa ntchito zake.

وددت أني كنت كبشا، فيذبحني أهلي، فيأكلون لحمي، ويحسون مرقي.

“Ndikulakalaka ndikadakhala nkhosa. Ondipha akadandipha, akanadya nyama yanga ndikumwa nsuzi wanga. (Siyaru Aa’laamin Nubalaa 3/14)

M’mawu ena, kuopa Allah Ta’ala ndikukhala ndi wamantha kuti adzayenera kuweruzidwa pazimene adachita kudali kwakukulu kwambiri kotero kuti adalakalaka kuti akanakhala nkhosa kuti asadzayankhe pa ntchito zake za tsiku ndi tsiku pa tsiku lachiweruzo.

Check Also

Zichitochito za Abu Ubaidah (Radhwiyallahu ‘anhu) Zigwirizana ndi Quraan Majiid

Pankhondo ya Badr, bambo a Abu Ubaidah Radhwiyallahu anhu adapitiriza kumulondora kufuna kuti amuphe. Komabe, …