Miswak

Nthawi Zimene Miswak Ikufunika Kugwirtsidwa Ntchito

7. Pamene wina ali kumapeto kwa moyo wake (ali pafupi kumwalira).

Sayyidatuna Aisha (radhiyallahu anha) akufotokoza kuti, Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) atatsala pang’ono kumwalira nchimwene wanga amene ndi AbdulRahmaan (radhiyallahu anhu) adalowa mchipinda chomwe Mtumiki (sallallah alaih wasallam) adagona atanyamula miswaak yomwe ankagwiritsa ntchito kutsukira mkamwa.

Read More »

Nthawi Zimene Miswak Ikufunika Kugwirtsidwa Ntchito

4. Pamene mukupanga wuzu.

Sayyiduna Abu Hurairah (radhiyallahu anhu) akuakufotokoza kuti Mtumiki (sallallahu alaih Wasalaam) adati, “chikhala kuti sichipsinjo pa ummah wanga ndikadawalamula (ndikadazipanga kukhala zokakamiza) kuti adzigwiritsa ntchito miswaak nthawi inailiyonse pamene akupanga wudhu (komano Sizili zokakamiza kutero koma ndisunnah yomwe yalimbikitsidwa pamene mukupanga wudhu).”

Read More »

Njira Ya Sunnah Yogwiritsira Ntchito Miswaak (mswachi ochokera ku mtengo)

4. Mukatsiriza kugwiritsa ntchito miswaak, utsukeni ndipo uyikeni choimika.[1] 5. Ngati palibe Miswaak, Chala sichingalowe m’malo mwa miswak, Kotero munthu adzayenera kugwiritsa ntchito chinthu chokhuthala chimene chingathe kuyeretsa mkamwa, monga nswachi (toothbrush).[2] 6. Miswaak siwoyenera kuti utali wake upambane chikhatho chadzanja limodzi.[3] 7. Kamtengo kali konse komwe kamakhala bwino kuchukuchira …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yogwiritsira Ntchito Miswaak (mswachi ochokera ku mtengo)

1. Njira yogwilira miswaak ili motere, Munthu ayenere ayike chala chachikulu ndi chaching´ono pansi pa miswaak ndipo zala zake zotsalazo ayike mbali yapamwamba pa Miswaak.[1] 2. Gwirani Miswaak ndi mkono wamanja ndipo yambani kutsuka mano kuyambira mbali yakumanja.[2] 3. Tsukani mano mopingasa ndipo lilime mulitsuke molitsatira (mulitali make), chimodzimodzinso, tsukani …

Read More »

Ubwino ogwiritsa ntchito miswak

1. Kugwiritsa ntchito miswak kumaonjezera sawaabu za swalah ka 70.

Sayyiduna Aaishah radhiyallahu anha akunena kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati, swalah imene yapempheledwa utagwiritsa ntchito miswak (popanga wudhu) ilindi sawaab zokwana 70 kuposa swalah yomwe yaswalidwa popanda kugwiritsa ntchito miswak.

Read More »