12. Kenako udzayamba kuwerenga surah Faatihah ndi surah ina kapena gawo lina la Quraan Majeed. Musanayambe kuwerenga surah faatihah, werengani tasmiyah chifukwa ndi gawo la surah fatihah. Tasmiyah ndi kuwerenga: بسم اللهِ الرَّحْمنِ الرَّحِيمِ M’dzina la Allah, Wachifundo chambiri, Wachisoni. Dziwani izi: Ngati ndiwe Imaam, werenga tasmiyah mokweza mu Swalaah …
Read More »Qiyaam
10. Mukangoiyamba swalah yanu werengani Duaa-ul Istiftaa chamuntima. وَجَّهْتُ وَجْهِيَ لِلَّذِيْ فَطَرَ السَّمَاوَاتِ وَالْأَرْضَ حَنِيْفًا مُسْلِمًا وَمَا أَنَا مِنَ الْمُشْرِكِيْنَ إِنَّ صَلَاتِيْ وَنُسُكِيْ وَمَحْيَايَ وَمَمَاتِيْ لِلّٰهِ رَبِّ الْعَالِمِيْنَ لَا شَرِيْكَ لَهُ وَبِذلِكَ أُمِرْتُ وَأَنَا مِنَ الْمُسْلِمِيْنَ Ndikuyang’ana nkhope yanga kwa Yemwe adalenga thambo ndi nthaka, ndikukhala panjira yoongoka popanda kusokonekera, …
Read More »Qiyaam
7. Nthawi yowerenga Takbiiratul ihraam (Takbiir-e-Tahriimah) onetsetsani kuti maso anu a kuyang’anaya malo opanga Sajdah ndikupendamitsa mutu wanu pang’ono pansi.[1] 8. Ikani dzanja lanu lamanja pa dzanja lanu lamanzere ndikuwaika pansi pa chidali pamwamba pa nchombo.[2] 9. Gwirani joini yanu ya dzanja lamanzere ndi dzanja lanu lamanja, zala zanu zakumanja …
Read More »Qiyaam
1. Pamene mukufuna kuswali, imani ndi kuyang’ana pa Qiblah.”[1] 2. Poimirira kuti muswali, imani molemekeza kwambiri. Yang’anizani mapazi onse ku Qiblah ndipo sungani mpata wa pafupifupi dzanja limodzi pakati pawo. Poswali pagulu, ongolani masafu (mizere) ndipo imani moyandikana momwe mungathere, popanda kusiya mipata pakati panu. Mapazi sayenera kupatukana m’njira yakuti …
Read More »Tisadaswali
6. Onetsetsani kuti mukuswali mutavala chisoti mmutu chifukwa idali sunnah ya Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) komanso ma swahabah (radhwiyallahu anhum) kuvala chisoti akamaswali. روي عن ابن عباس رضي الله عنهما أن رسول الله صلى الله عليه وسلم كان يلبس القلانس تحت العمائم ويلبس العمائم بغير القلانس (جمع الوسائل صـ 207)[1] …
Read More »Tisadaswali
1. konzekerani za swalah nthawi yabwino ndi kuonetsetsa kuti simunazikonzekeretse thupi lokha koma ndi maganizo omwe mwakonzeka zoti mukukaima pamanso pa Allah.[1] 2. onetsetsani kuti mukupemphera swalah iliyonse munthawi yake komanso mwakaswali pagulu ku mnzikiti.[2] عن أبي هريرة رضي الله عنه قال قال رسول الله صلى الله عليه وسلم لولا …
Read More »Mmene Ma Swahaabah Ankachitira Zokhudza Salaah Yapagulu
Sayyiduna Abdullah bin Masuud (radhwiyallahu anhu) zikunenedwa kuti iye adati: “Sungani Swalah zanu zisanu pa tsiku popemphera pa malo amene adhaan yaitanidwa (monga musjid). Ndithu, Swalah izi (Fardh) m’Musjid ndi zochokera ku Sunan huda (mapembedzedwe olamuridwa mu Deen). Allah wamulamula Nabiy wake sunan huda (mapembedzedwe amenewa ndi chiongoko kwa inu). …
Read More »Malangizo Kwa Amene Amanyalanyaza Swalaah Ya Pagulu Jamaat Mu Mzikiti
Lidali khumbo la Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) kuti amuna onse a Ummah wake adzipempelera swalah zawo ku mzikiti pa jamaa Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) ankakhudzidwa kwambiri akazindikira kuti munthu wina wake wapemphelera kunyumba ndipo adati: “Pakadapanda kupezeka kwa akazi ndi ana, ndikadalamula gulu la achinyamata kuti lisonkhanitse nkhuni ndi kuyatsa …
Read More »Nthawi Yoyenera Ndi Kachitidwe Koyenera
Monga momwe Swalah ilili yofunika, kuiswali mu nthawi yoyenera komanso moyenera ndikofunikanso. Sayyiduna Mtumiki (Swallallahu alaih wasallam) adati: “Munthu akapemphera Swalaah mu nthawi yake yoikika ndi wudhu woyenerera, kukwaniritsa qiyaam (kuimirira), rukuu ndi sajdah m’njira yolondora ndi mlingo wofunika okhazikika ndi kudzipereka, kenako Swala imadzuka mowala bwino ndikumuuza kuti: Allah …
Read More »Salaah Ya Amuna
Udindo wapamwamba womwe Swalah ili nawo m’moyo wa Msilamu siufunikira kufotokoza kulikonse. Mfundo yoti idzakhala gawo loyamba lomwe adzafunsidwe munthu pa tsiku la Qiyaamah ndi umboni wokwanira wotsimikizira kufunika kwake. Sayyiduna Rasulullah (swallallahu alaih wasallam) إن أول ما يحاسب الناس به يوم القيامة من أعمالهم الصلاة قال يقول ربنا جل …
Read More »