Daily Archives: July 8, 2026

Kuyamika Pa Mdalitso Okhala Ndi Moyo

Dawuud bin Dinaar anali Imaam wamkulu pankhani ya Hadith komanso mphunzitsi wa ma Muhadditheen otchuka, monga Imaam shu’bah (rahimahullah) ndi Imaam Wakii (rahimahullah). Mkatikati mwa moyo wake kunadzabuka mliri ku Khuraasaan kumene ankakhala omwe udakhudza anthu ndipo ambiri adataya miyoyo yawo. Dawuud bin Dinaar (rahimahullah) anali m’gulu la omwe adagwidwa …

Read More »