Rasulullah (Swallallahu ‘alaihi wasallam) pomutumiza Mu’aaz (radhwiyallahu ‘anhu) ku Yemen, adamufunsa kuti, “Ndi njira yanji yomwe udzatsatire ukamakapereka chigamulo pa nkhani za Asilamu?” Mu’aaz (Radhwiyallahu ‘anhu) adayankha kuti: “Ndidzagwiritsa ntchito Qur’aan.” Kenako Nabi (Swallallahu ‘alaihi wasallam) adamufunsa kuti: “Ngati lamulo silikupezeka mu Qur’aan udzatani?” Iye adayankha kuti, “Ndidzagwiritsa nctchito mahaadith …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu