Daily Archives: August 25, 2026

kuzindikira kwakukulu kwa Abdullah bin Abbaas (radhiwyallahu ‘anhuma)

Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) akuti: Mtumiki wa Allah (swallallahu ‘alaihi wasallam) atamwalira, ndinauza mnzanga wina wachi Ansaari kuti, “Bwera, tiye tipite tikaphunzire (Dini) kuchokera kwa Ma Sahaabah (radhwiyallahu ‘anhum), pomwe ambiri a iwo akadalipo pakati pathu.” Anandiyankha kuti, “Iwe Ibnu Abbaas! Ndikulumbira mwa Allah, ndikudabwa kuti ukuganiza kuti …

Read More »