Said bin Abi Sa’eed Al-Maqburi (rahimahullah) akufotokoza izi: Tsiku lina tidali limodzi ndi Abu Hurairah (Radhwiyallahu ‘anhu) pamene Hasan bin ‘Ali (Radhwiya Allaahu ‘anhu) adadza kwa ife natilonjera ndi salaamu. Gulu lomwe lidamuzungulira Abu Hurairah (Radhwiya Allaahu ‘anhu) adamumva akupereka salamu kwa iwo ndipo adamuyankha. Pambuyo pake, Hasan (Radhwiyallahu ‘anhu) …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu