Daily Archives: November 24, 2026

Kufunsa Maganizo Kwa Ma Ulama Olungama

Mfundo yoti “Funsani akatswiri a ntchitoyi” ndi mfundo yomwe imatchulidwa kawirikawiri komanso kugwiritsidwa ntchito m’magawo onse a moyo. Taganizirani chitsanzo cha munthu amene akufuna kumanga nyumba yosanjikizana patatu. Kodi ndi njira ziti zomwe angatsatire kuti akwaniritse cholinga chake? Choyamba adzalankhula ndi katswiri wa zomangamanga kuti ajambule pulani. Pambuyo pake, adzalemba …

Read More »