Munthu Wachikulire Okhala ndi invi
Olemekezeka Anas (Radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) adati: “Ndithu Allah amachita manyazi kukana duwa ya munthu (okalamba) watsitsi loyera ngati ali olungama
Munthu Opanga Dua Pagulu
Olemekezeka Habiib bun Maslamah (Radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) adati: “Palibe gulu la anthu lomwe lingasonkhane, kenako wina mwa iwo ndikumapanga duwa ena ndikumavomera kuti Aamiin, kupatura kuti Allah amalandira duwa yawo.”
[1] المعجم الأوسط للطبراني، الرقم: 5286، وقال العلامة الهيثمي رحمه الله في مجمع الزوائد، الرقم: 17213: وفيه صالح بن راشد وثقه ابن حبان وفيه ضعف وبقية رجاله ثقات
[2 المستدرك على الصحيحين للحاكم، الرقم: 5478، وقال العلامة الهيثمي رحمه الله في مجمع الزوائد، الرقم: 17347: ورجاله رجال الصحيح غير ابن لهيعة وهو حسن الحديث