6. Yang’anani ku Qiblah pamene mukupanga Adhaan.[1] عن معاذ بن جبل رضي الله عنه قال … فجاء عبد الله بن زيد رجل من الأنصار وقال فيه فاستقبل القبلة … (سنن أبي داود، الرقم: 507)[2] Sayyiduna Mu’adh bin Jabal (radhiyallahu anhu) akusimba kuti, “…Sayyiduna Abdullah bin Zaid (radhiyallahu anhu) amene adali …
Read More »Monthly Archives: November 2021
Chiyambi Chakuwala Kwa Munthu Patsiku Lachiweruzo
عن ابن عمر رضي الله عنهما قال قال رسول الله صلى الله عليه وسلم زينوا مجالسكم بالصلاة علي فإن صلاتكم علي نور لكم يوم القيامة (الفردوس بمأثور الخطاب، الرقم: ٣٣٣٠، وإسناده ضعيف كما في القول البديع صـ 278) Sayyiduna Ibnu Umar (radhiyallahu anhu) akusimba kuti, Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati …
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
4. Kupanga Adhaana ndimau okweza kwambiri.
Sayyiduna Abdullah mwana wa Zaydu (radhiyallah anhu) akusimba kuti ...... Kenako ndinamuuuza Mtumiki (sallallah alayhi wasallam zamaloto amene ndidalota (komanso kapangidwe ka adhaana kamene ndinaphunzitsidwira mmalotomo).Mtumiki (sallallah alayhi wasallam) adayankha nati; Ndithudi ndimaloto owona inshaa Allah, Pita kwa Bilaal radhiyallah anhu ukamphunzitse mawu aadhaana amene wamva mmaloto ako kuti naye adzipanga adhaana pogwiritsa ntchito mawu amenewa, Chifukwa choti Bilaliyo mawu ake ndiokwera kwambiri kuposa mawu ako.
Read More »Chizindikiro chokhala ndi makhalidwe oipa komanso kusayamika
عن قتادة رحمه الله قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: من الجفاء أن أذكر عند الرجل فلا يصلي علي (الإعلام بفضل الصلاة على النبي صلى الله عليه وسلم للنميري، الرقم: ٢٠٩، ورواته ثقات كما في القول البديع صـ ٣١١) Sayyiduna Qataadah (rahimahullah) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahua alaih wasallam) …
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
1. Onetsetsani kuti chitsimikizo chanu chopangira adhaana chikhale kusangalatsa Allah Taala basi. عن ابن عباس رضي الله عنهما أن النبي صلى الله عليه وسلم قال من أذن سبع سنين محتسبا كتبت له براءة من النار (سنن الترمذي، الرقم: 206)[1] Sayyiduna Ibn Abbas Allah asangalare naye akunena kuti; Bwana wathu Mtumiki …
Read More »Kusiya ntchito yomwe ingakakulowetse ku Jannah
Sayyiduna Husain bin Aliy (radhiyallahu anhuma) akufotokoza kuti Mthenga wa Allah madalitso ndi ntendere zipite kwa iye adati: munthu amene dzina langa latchulidwa pamaso pake ndiye osandifunira zabwino (osawerenga Durood) munthu ameneyo wasiya ntchito yabwino yokakulowetsa ku Jannah.
Read More »Mbiri Za Muadhin
1. Munthu ochita adhana (muadhin) akuyenera akhale wamwamuna.[1] عن ابن عمر رضي الله عنهما قال ليس على النساء أذان ولا إقامة (السنن الكبرى للبيهقي، الرقم: 1996)[2] Zikunenedwa kuti Olemekezeka Ibn umar (radhiyallah anhuma) adati; “Kupanga azaana ndi iqaamah siudindo wa azimayi ayi” 2. Akhale wanzeru (ozindikira zomwe akuchita).[3] 3. Akhale …
Read More »Kupeza nawo pempho la Mtumiki (sallallahua alaih wasallam)
عن ابن عمر عن النبي صلى الله عليه وسلم قال من زار قبري بعد موتي كان كمن زارني في حياتي (المعجم الأوسط، الرقم: 287) رواه الطبراني والدارقطني والبيهقي وضعفه كذا في الإتحاف وفي المشكوة برواية البيهقي في الشعب بلفظ : من حج فزار قبري بعد موتي كان كمن زارني في …
Read More »Ubwino wa Muadhin
9. Chidali chikhumbokhumbo cha maswahaba (radhiyallahu anhum) kuti azipanga adhaana ndiponso ankalakalaka kuti ana awonso azipanga adhaana. Mmusimu muli ena mwamahadith amene akuonetseratu poyera kufunitsitsa kwa maswahaba kuti nawo adzipanga adhaana: kufunisitsa kwa Olemekezeka Ali radhiyallahu anhu kuti ana ake Hassan ndi Hussein (Radiyallah anhumaa) azipanga adhaana. عن علي رضي …
Read More »