Monthly Archives: September 2025

Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) Amva kuyenda kwa Mapazi a Olemekezeka Bilaal (Radhwiya Allaahu ‘anhu) ku Jannah.

Olemekezeka Abu Hurairah (Radhwiya Allaahu ‘anhu) akusimba kuti nthawi ina, nthawi ya Swalah ya Fajr, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) adati kwa Bilaal (Radhwiyallahu ‘anhu): “E, Bilaal! Pa ntchito zabwino zomwe umachita mchisilamu, ndi ntchito iti yomwe imakulimbikitsa kuti udzapindula nayo pa tsiku lachiweruzo,chifukwa usiku wapitawu ndamva kuyenda …

Read More »