وَالنَّازِعَاتِ غَرْقًا ﴿١﴾ وَالنَّاشِطَاتِ نَشْطًا ﴿٢﴾ وَالسَّابِحَاتِ سَبْحًا ﴿٣﴾ فَالسَّابِقَاتِ سَبْقًا ﴿٤﴾ فَالْمُدَبِّرَاتِ أَمْرًا ﴿٥﴾ Ndikulumbirira (angelo) amene amachotsa (mizimu ya osakhulupirira) mwaukali, ndi (angelo) amene amachotsa (miyoyo ya okhulupirira) moleza, ndi (Angelo) amene amasambira nayo mizimuyo (m’mlengalenga), ndi (Angelo) amene amapikisana (kukwaniritsa malamulo a Allah Ta’ala). Monga ziliri kuti Sura Nabai idavumbulutsidwa kuti idzakhazikitse chikhulupiriro cha tsiku la …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu