Khalidwe lake Asanalowe Chisilamu: Asanalowe Chisilamu, Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu) anali chigawenga. Anali olimba mtima kwambiri kotero kuti popanda kuthandizidwa ndi anzake ena, ankakwanitsa yekha kubera anthu ndikuwachita uchifwamba. Nthawi zina, ankaukira anthu apaulendo atakwera pahatchi, ndipo nthawi zina, ankaukira akuyenda pansi. (Siyar A’laam min Nubalaa 3/373) Pambuyo pake, anasiya …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu