Olemekezeka Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu) atatsala pang’ono kumwalira, panalibe wina aliyense kupatula mkazi wake ndi kapolo wake. Anawalangiza kuti, “Mundisambitse ndi kundiveka sanda (ndikamwalira). Kenako tengani thupi langa ndi kuliyika pamsewu. Uzani gulu la anthu lomwe liyambilire kudutsa kuti, “Uyu ndi Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu),Otsatira wa Rasulullah (swallallahu ‘alayhi wasallam). …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu