1. Mulimbikire kuchita ibaadah m’masiku khumi oyambirira a Zul Hijjah. Malipiro aakulu atchulidwa pa ibaadah yomwe ingachitike m’masiku khumi amenewa. Olemekezeka Abdullah bin Abbaas radhwiyallahu anhu wanena kuti Nabiy swallallahu alaihi wasallam adati: “Palibe cholungama chomwe chingachitike tsiku lililonse la chaka chomwe chili chabwino kwambiri kuposa masiku khumi a mwezi …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu