Yearly Archives: 2022

Nsembe ya maswahabah radhwiyallahu anhum pa Mtumiki (swallallahu alaih wasallam)

Nyumba ya Bibi Faatimah (radhiyallahu anha) idali potalikirako ndi nyumba ya Mtumiki (sallallahu alaih wasallam). Tsiku lina Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adamuuza kuti “khumbo langa ndiloti udzikhala nane pafupi” Bibi Faatimah (radhiyallahu anha) adayankha nati, Nyumba ya Haarithah ili pafupi ndi yanu, ngati mungamupemphe kuti tisinthanitse ndi yanga adzavomera mwansangala. …

Read More »

Tafseer Ya Surah Quraish

لِإِيلفِ قُرَيْشٍ ‎﴿١﴾‏ اِلٰفِهِمْ رِحْلَةَ الشِّتَآءِ وَالصَّيْفِ ‎﴿٢﴾‏ فَلْيَعْبُدُوا۟ رَبَّ هٰذَا الْبَيْتِ ‎﴿٣﴾‏ الَّذِىٓ أَطْعَمَهُم مِّن جُوْعٍ وَاٰمَنَهُمْ مِّنْ خَوْفِۭ ‎﴿٤﴾‏ Chifukwa cha chitetezo cha ma Quraishi, chitetezo chimene amasangalala nacho m’maulendo awo m’miyezi yachisanu ndi m’nyengo yachilimwe. Kotero akuyenera kupembedza Mbuye wa nyumba yopatulika (Ka’aba), yemwe adawapatsa chakudya chothetsa njala yawo ndi chitetezo ku …

Read More »

Kuwerenga Duruud ngati waiwala China chake

عن أنس رضي الله عنه قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: إذا نسيتم شيئا فصلوا علي تذكروه إن شاء الله تعالى (أخرجه أبو موسى المديني بسند ضعيف كما في القول البديع صـ 448) Sayyiduna Anas (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) adati: ngati waiwala chinachake udziwerenga …

Read More »

Tisadaswali

1. konzekerani za swalah nthawi yabwino ndi kuonetsetsa kuti simunazikonzekeretse thupi lokha koma ndi maganizo omwe mwakonzeka zoti mukukaima pamanso pa Allah.[1] 2. onetsetsani kuti mukupemphera swalah iliyonse munthawi yake komanso mwakaswali pagulu ku mnzikiti.[2] عن أبي هريرة رضي الله عنه قال قال رسول الله صلى الله عليه وسلم لولا …

Read More »

Palibe malo mu Chisilamu kwa amene a kunyoza ma Swahaabah (Radhiyallahu anhum)

Tsiku linalake Munthu wina anafika kwa Zainul Aabidiin, Aliy bin Husain rahimahullah ndipo adafunsa: Oh chidzukulu cha Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) maganizo anu ndi otani pa nkhani ya Uthmaan (radhwiyallahu anhu)? Atazindikira za nkwiyo wa munthuyu pa Uthmaan (radhwiyallahu anhu, Olemekeza Zainul Aabidiin (rahimahullah)adamulongosolera munthuyo kuti: Oh m’bale wanga okondeka! …

Read More »

Mmene Ma Swahaabah Ankachitira Zokhudza Salaah Yapagulu

Sayyiduna Abdullah bin Masuud (radhwiyallahu anhu) zikunenedwa kuti iye adati: “Sungani Swalah zanu zisanu pa tsiku popemphera pa malo amene adhaan yaitanidwa (monga musjid). Ndithu, Swalah izi (Fardh) m’Musjid ndi zochokera ku Sunan huda (mapembedzedwe olamuridwa mu Deen). Allah wamulamula Nabiy wake sunan huda (mapembedzedwe amenewa ndi chiongoko kwa inu). …

Read More »

Mphavu za Aliyy (radhiyallahu anhu) pa nkhondo ya Uhud

Pa nkhondo ya Uhud ma swahabah (radhwiyallahu anhum) adagonjetsedwa kwambiri ndi adani ndipo ambiri adaphedwa kumene, Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) Adazunguliridwa ndi adani ndikuvulazidwa kwambiri, nthawi imeneyi mphekesera idayamba kumveka kuti Mtumiki waphedwa, maswahabah atamva mphekesera imeneyi adasweka mitima ndikutaya chiyembekezo. Hazrat Ali (radhwiyallahu anhu) akufotokoza kuti: tidazunguliridwa ndi adani …

Read More »

Malangizo Kwa Amene Amanyalanyaza Swalaah Ya Pagulu Jamaat Mu Mzikiti

Lidali khumbo la Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) kuti amuna onse a Ummah wake adzipempelera swalah zawo ku mzikiti pa jamaa Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) ankakhudzidwa kwambiri akazindikira kuti munthu wina wake wapemphelera kunyumba ndipo adati: “Pakadapanda kupezeka kwa akazi ndi ana, ndikadalamula gulu la achinyamata kuti lisonkhanitse nkhuni ndi kuyatsa …

Read More »

Olemekezeka Talhah (radhwiyallahu anhu) pa nkhondo ya Uhud

Olemekezeka Zubair bin Awwaam (radhwiyallahu anhu) akufotokoza kuti pa nkhondo ya Uhud Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) adaphatikiza zovala zozitetezera pa nkhondo. Mkatikati mwa nkhondo Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) adafuna kukwera miyala ikulu ikulu koma ankakanika chifukwa chakulemera kwa zovala za pa nkhondo.Choncho adamupempha Olemekezeka Talha (radhwiyallahu anhu) kuti akhale pansi …

Read More »

Nthawi Yoyenera Ndi Kachitidwe Koyenera

Monga momwe Swalah ilili yofunika, kuiswali mu nthawi yoyenera komanso moyenera ndikofunikanso. Sayyiduna Mtumiki (Swallallahu alaih wasallam) adati: “Munthu akapemphera Swalaah mu nthawi yake yoikika ndi wudhu woyenerera, kukwaniritsa qiyaam (kuimirira), rukuu ndi sajdah m’njira yolondora ndi mlingo wofunika okhazikika ndi kudzipereka, kenako Swala imadzuka mowala bwino ndikumuuza kuti: Allah …

Read More »