Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (Radhiya Allaahu ‘anhuma) akusimba kuti nthawi ina iye adali ndi bambo ake pamaso pa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) pomwe Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) ankakambirana ndi mumthu wina mwamseri. Popeza kuti Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu