Adhaan Ndi Iqaamah

Mawu a Adhaan

Mu Adhaan muli magawo amawu okwana asanu ndi awiri, mawu asanu ndi awiriwa atchulidwa mmusimu:[1] 1. Poyamba mudzanena mawu awa: اَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ Allah ndi wankulu, Allah ndi wankulu اَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ Allah ndi wankulu, Allah ndi wankulu 2. Pachiwiripa mudzanena mawu anayi awa koma mudzayamba ndikunena motsitsa …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

15. Ngati muli malo oti ndi otalikirana ndi midzi kapena mchipululu komwe kulibe munthu oti mutha kupemphera naye, ngakhale mutakhala kuti muswali nokha mukuyenerabe kupanga Adhaan ndi Iqaamah, ngati mungapange Adhaan komanso Iqaamah kenako ndikuyamba kuswali, angelo adzaswali nanu limodzi.[1] عن عقبة بن عامر رضي الله عنه قال سمعت رسول …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

14. Siyani nthawi yokwanirab pakati pa Adhaan ndi Iqaamah ndicholinga choti anthu akhoza kukhala ndi nthawi yokwanira yozikhonzekeretsa, chipindi cha Maghrib chidzapempheredwa kungomaliza Adhaan.[1] عن جابر رضي الله عنه أن رسول الله صلى الله عليه وسلم قال لبلال إذا أذنت فترسل وإذا أقمت فاحدر واجعل بين أذانك وإقامتك قدر ما …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

11. Musayankhule pamene mukupanga Adhaan.[1] 12. Musasokoneze mawu Adhaan kapena kupanga kusintha mawu mmatchuridwe.[2] عن يحيى البكاء قال قال رجل لابن عمر رضي الله عنهما إني لأحبك في الله فقال ابن عمر رضي الله عنهما لكني أبغضك في الله قال ولم قال إنك تتغنى في أذانك وتأخذ عليه أجرا (مجمع …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

9. Lowetsani zala zanu za nkomba phala m’makutu mwanu pamene mukupanga Adhaan.

Sayyiduna Sa’d Al-Qurazi (radhiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adamuuza Bilaal (radhiyallahu anhu) kuti alowetse zala zake m’makutu mwake (pamene ankapanga Adhaan) ndip adati “izi zizikuthandiza kuti udzikweza mawu kwambiri popanga Adhaan.”

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

6. Yang’anani ku Qiblah pamene mukupanga Adhaan.[1] عن معاذ بن جبل رضي الله عنه قال … فجاء عبد الله بن زيد رجل من الأنصار وقال فيه فاستقبل القبلة … (سنن أبي داود، الرقم: 507)[2] Sayyiduna Mu’adh bin Jabal (radhiyallahu anhu) akusimba kuti, “…Sayyiduna Abdullah bin Zaid (radhiyallahu anhu) amene adali …

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

4. Kupanga Adhaana ndimau okweza kwambiri.

Sayyiduna Abdullah mwana wa Zaydu (radhiyallah anhu) akusimba kuti ...... Kenako ndinamuuuza Mtumiki (sallallah alayhi wasallam zamaloto amene ndidalota (komanso kapangidwe ka adhaana kamene ndinaphunzitsidwira mmalotomo).Mtumiki (sallallah alayhi wasallam) adayankha nati; Ndithudi ndimaloto owona inshaa Allah, Pita kwa Bilaal radhiyallah anhu ukamphunzitse mawu aadhaana amene wamva mmaloto ako kuti naye adzipanga adhaana pogwiritsa ntchito mawu amenewa, Chifukwa choti Bilaliyo mawu ake ndiokwera kwambiri kuposa mawu ako.

Read More »

Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana

1. Onetsetsani kuti chitsimikizo chanu chopangira adhaana chikhale kusangalatsa Allah Taala basi. عن ابن عباس رضي الله عنهما أن النبي صلى الله عليه وسلم قال من أذن سبع سنين محتسبا كتبت له براءة من النار (سنن الترمذي، الرقم: 206)[1] Sayyiduna Ibn Abbas Allah asangalare naye akunena kuti; Bwana wathu Mtumiki …

Read More »

Mbiri Za Muadhin

1. Munthu ochita adhana (muadhin) akuyenera akhale wamwamuna.[1] عن ابن عمر رضي الله عنهما قال ليس على النساء أذان ولا إقامة (السنن الكبرى للبيهقي، الرقم: 1996)[2] Zikunenedwa kuti Olemekezeka Ibn umar (radhiyallah anhuma) adati; “Kupanga azaana ndi iqaamah siudindo wa azimayi ayi” 2. Akhale wanzeru (ozindikira zomwe akuchita).[3] 3. Akhale …

Read More »

Ubwino wa Muadhin

9. Chidali chikhumbokhumbo cha maswahaba (radhiyallahu anhum) kuti azipanga adhaana ndiponso ankalakalaka kuti ana awonso azipanga adhaana. Mmusimu muli ena mwamahadith amene akuonetseratu poyera kufunitsitsa kwa maswahaba kuti nawo adzipanga adhaana: kufunisitsa kwa Olemekezeka Ali radhiyallahu anhu kuti ana ake Hassan ndi Hussein (Radiyallah anhumaa) azipanga adhaana. عن علي رضي …

Read More »