Nthawi ya Hudaybiyah, Hazrat Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) adatumidwa ndi Rasulullah (sallallahu alaih wasallam) kukakambirana ndi ma Quraish ku Makka Mukarramah. Pamene Hazrat Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) adanyamuka kupita ku Makka Mukarramah, ena mwa maswahabah adamchitira kaduka Uthmaan (radhiyallahu anhu) chifukwa chokwanitsa kuchita tawaaf ya nyumba ya Allah (ka’bah). Komano mthenga …
Read More »Chikondi chakuya komanso chikumbutso cha Umar (radhwiyallahu anhu pa Mtumiki (swallallahu alaih wasallam)
Usiku wina olemekezeka Umar (radhwiyallahu anhu) mu ulamuliro wake ali mkati moyendayenda kupereka chitetezo adaona kuwala kuchokera nyumba inayake komanso adamva mawu. Atapita komweko adapeza mayi wachikulire akuluka uku akulakatula ndakatulo iyi, عَلَى مُحَمَّدٍ صَلَاةُ الْأَبْرَارْ ** صَلَّى عَلَيْكَ الْمُصْطَفَوْنَ الْأَخْيَارْ Ndikuppha anthu onse olungama kuti apitirize kumfunira zabwino Mtumiki …
Read More »