Sayyiduna Abu Dardaa (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati, “munthu amene angandifunire zabwino pondiwerengera Durood kokwana ka khumi m’mawa ulionse komanso kumadzulo kulikonse adzapeza nawo pempho langa la Shafaa patsiku lachiweruzo.”
Read More »Yearly Archives: 2021
Sunnah yosala kudya tsiku la Ashurah
Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) mwini wake adasala kudya tsiku la Ashurah ndikulambikitsanso maswahabah kuti asale kudya patsiku limeneli, khumbo lofuna kukwaniritsa sunnah imeneyi tingainvetse bwino kudzera mu Hadith iyi:
Read More »Zikhulupiliro Zokhudza Atumiki a Mulungu alaihim Salaam
6. Kuchuluka kwa aneneri onse akudziwa ndi Allah yekha, timakhulupilira mwa atumiki onse angakhale ochuluka bwanji. 7. Monga ziliri kuti ndi chizindikiro cha utumiki, Allah amamulora mtumiki kuchita zodabwitsa zomwe zimatchedwa kuti Mu’ujizaat. Komano Tikuyenera kuzindikira kuti mtumiki ndi munthuso ndipo sangapange zodabwitsa mwa iye yekha, zimangochitika kudzera muchifuniro cha …
Read More »Muharram ndi Ashurah
Ndi dongosolo la Allah Ta’ala kuti anadalitsa zinthu zina kuposa zinzake, mwa anthu onse, aneneri ndi omwe adadalitsika kwambiri popatsidwa ulemelero wa pamwamba kwambiri kuposa anthu ena onse, malo onse osiyanasiyana omwe alipo padziko lapansi pano Allah adaidalitsa haramain (Makkah Mukarramah ndi Madinah Munawwarah) kuphatikizapo Aqsa, ndipo pa miyezi 12 …
Read More »Zikhulupiliro Zokhudza Atumiki a Mulungu (alaihim Salaam)
1. Allah Ta’ala adatumiza atumiki osiyanasiyana kumayiko kuti awatsogolere anthu kunjira yowongoka.[1] 2. Mtumiki ankachita kusankhidwa ndi Allah Ta’ala. Allah Ta’ala ankasankha mwa akapolo ake amene wamufuna pantchito yotamandikayi. Utumiki sungapezeke ndimunthu aliyense kudzera mu ntchito zake ndikulimbikira kwake ayi (koma umachokera kwa Allah Taala).[2] 3. Mtumiki amene adapatsidwa bukhu …
Read More »Kuwerenga Durood Musadayambe Kupanga Duwa
عن عبد الله بن مسعود قال إذا أراد أحدكم أن يسأل فليبدأ بالمدحة والثناء على الله بما هو أهله ثم ليصل على النبي صلى الله عليه وسلم ثم ليسأل بعد فإنه أجدر أن ينجح (المعجم الكبير للطبراني، الرقم: ٨٧٨٠، ورجاله رجال الصحيح إلا أن أبا عبيدة لم يسمع من أبيه …
Read More »Nthawi Zimene Miswak Ikufunika Kugwirtsidwa Ntchito
1. Mukangodzuka kumene.
Sayyiduna Aishah radhiyallahu anha akusimba kuti, nthawi zonse Mtumikisallallahu alaih wasallam ankati akadzuka, kaya ndimasana kapena usiku ankatsuka mkamwa ndi miswak asanapange wudhu.’’
Read More »Zikhulupiliro Zokhudza Mtumiki Wa Allah Muhammad (Sallallah alayhi wasallam)
5. Allah Ta’ala adamudalitsa Mtumiki (sallallah alayhi wasallam) ndi zabwino zapadera zimene Atumiki ndi aneneri a Mulungu sadapatsidwe. Mtumiki (salallah alayhi wasallama) akusimba kuti:
(Ndadalitsidwa ndi zinthu zisanu ndi chimodzi (6), zimene atumiki akale sadapatsidwepo, Ndadalitsidwa popatsidwa jawaamil al kalaam (Mau amodzi koma amatanthauzo ochuluka, mwachitsanzo Quran yolemekezeka komanso mahadith olemekezeka muli matanthauzo akuluakulu kuchokera mu mau ochepa),
Read More »
Kupeza duwa ya Mtumiki (sallallahua alaih wasallam) chifukwa chowerenga Durood pa tsiku la Jumuah
Sayyiduna Umar bin Khattwaab (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati: Chulukitsani kundiwerengera Durood pa tsiku la Jumuah popeza Durood yanu imafikitsidwa kwa ine ndipo kenako ndimakupangirani kupempha Allah kuti akukhululukireni machimo anu.
Read More »Njira Ya Sunnah Yogwiritsira Ntchito Miswaak (mswachi ochokera ku mtengo)
4. Mukatsiriza kugwiritsa ntchito miswaak, utsukeni ndipo uyikeni choimika.[1] 5. Ngati palibe Miswaak, Chala sichingalowe m’malo mwa miswak, Kotero munthu adzayenera kugwiritsa ntchito chinthu chokhuthala chimene chingathe kuyeretsa mkamwa, monga nswachi (toothbrush).[2] 6. Miswaak siwoyenera kuti utali wake upambane chikhatho chadzanja limodzi.[3] 7. Kamtengo kali konse komwe kamakhala bwino kuchukuchira …
Read More »