7. Osamwera mbali yomwe ndi yodulidwa kapena yosweka ya chikho, chifukwa ndizotheka kuti mutha kuvulala. Olemekezeka Abu Sa’eed Khudri (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adamuletsa munthu wina kumwera mbali ya chikho yophwanyika kapena kusweka. 8. Musauzire m’pweya m’chiwiya. Sayyiduna Ibnu Abbaas (radhwiyallahu anhuma) akunena kuti Rasulullah (swallallahu …
Read More »Sunnats Ndi Aadaab Pa Kumwa 1
1)Musanamwe, Nenani dzina la Allah powerenga بِسْمِ الله M’dzina la Allah. 2) Imwani ndi dzanja lamanja. Olemekezeka Ibnu Umar radhwiyallah anhuma akunena kuti Rasulullah adati, “Aliyense wa inu akamayamba kudya, ayenera kudyera dzanja lake lamanja, ndipo akamamwa, ayenera kumwera dzanja lake lamanja, pakuti Shaitaan amadya ndi dzanja lake lamanzere ndi …
Read More »Kumwa
Pali ma sunnah ndi ma adaab ambiri okhudzana ndi kumwa. Ma sunnah ndi ma adaab ena amakhudzana ndi madua osiyanasiyana omwe alamulidwa kuti awerengedwe usanayambe kumwa, pamene ukumwa komanso utamaliza. Ma sunnah ndi ma adaab ena amakhudzana ndi momwe munthu angamwere. Kupatula izi, pali ma sunnah ndi ma adaab omwe …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu