Daily Archives: July 22, 2026

Tsiku La Chiweruzo – Tsiku Lodzakhudwa Kwa Anthu Ambiri

Mu Quraan Majid, Tsiku la Qiyaamah latchulidwa ndi mayina osiyanasiyana. Mayina ena mwa awa ndi “Tsiku la Mphotho ndi Kubwezera”, “Tsiku losonkhana”, “Tsiku la Kutayika ndi Kupindula” (lodzataika kwa osakhulupirira ndi la phindu kwa okhulupirira), ndi “Tsiku la Kukumana” (kutanthauza kukumana ndi Allah Talaa. Tikayang’ana mayina awa, timapeza kuti dzina …

Read More »