Daily Archives: July 20, 2026

Makhalidwe Abwino a Muaaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu)

Farwah bin Nawfal akufotokoza kuti nthawi ina yake, Abdullah bin Masud (radhwiyallahu anhu) adalankhula za Muaaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu) ndipo ankamuyamikira kwambiri chifukwa cha zabwino zomwe anali nazo. Iye adati: إن معاذا كان أمة قانتا لله حنيفا “Ndithu, Muaaz (bin Jabal) adali ummah (mtsogoleri wlotsogolera ena kunjira yoongoka), pomwe …

Read More »