1. Onetsetsani kuti mkamwa mwanu ndimoyera musanambe kuwerenga Qur’an Majiid. Kwanenedwa kuti Ali (radhwiyallahu anhu) adati: “Ndithu, pakamwa panu ndi njira ya Qur’an Majiid (pakamwa panu mumawerenga Qur’an Majiid). Pa chifukwa chimenechi, tsukani mkamwa mwanu pogwiritsa ntchito miswaak. 2. Inyamureni Quraan Majiid Mwaulemu kwambiri ndipo nthawi zonse iyikeni pamalo Olemekezeka …
Read More »Yearly Archives: 2024
Maloto a Sa’d (radhwiyallahu ‘anhu) Asanalowe Chisilamu
Sa’d (radhwiyallahu ‘anhu) anati: Ndisanalowe Chisilamu, ndinali ndi maloto omwe ndidawona ndili mumdima wandiweyani ndipo sanathe kuwona kalikonse. Mwadzidzidzi, panaoneka mwezi umene unayamba kuwala usiku. Kenako ndinatsatira kuwalako mpaka ndinakaufika mwezi M’malotowo, ndinaona ndithu anthu amene adanditsogolera kufikira mwezi. Ndidamuona Zaid bun Haarithah, Ali bun Abi Taalib ndi Abu Bakr …
Read More »Mariziq Ali M’manja Mwa Allah Yekha
Cholengedwa chilichonse chimafunikira kudya kuti chipitilire kukhala ndi moyo, ndipo chakudya chili m’manja mwa Allah yekha. Ziyenerezo, mphamvu ndi luntha sizizindikiro zodziwira umoyo wa munthu. Mawu a ndakatulo ndi oonadi: ينال الفتى من عيشه وهو جاهل ويكدى الفتى في دهره وهو عالم ولو كانت الأرزاق تجرى على الحجى هلكن إذا …
Read More »Ubwino Owerenga Quraan Majeed 3
Ntchito Yokondedwa Kwambiri Kwa Allah ndi Kuwerenga Qur’an mosalekeza Ibnu Abbaas (radhwiyallahu anhuma) akusimba kuti munthu wina adamufunsa Rasulullah swallallahu alaihi wasallam kuti, “Kodi ndi ntchito iti yomwe ili yokondedwa kwambiri kwa Allah? Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) anayankha kuti, ‘Ntchito za halaal ndi murtahil (wapaulendo amene akaima paulendo wake, amayambiranso …
Read More »Sayyiduna Ali (Radhwiyallaahu ‘anhu) kutumidwa ndi Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wasallam) kuti akakonze mitumbira ya Manda, kuswa Mafano ndi kufuta Zithunzi
Olemekezeka Ali (radhwiyallahu ‘anhu) akusimba kuti nthawi ina, Mtumiki (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adapita ku maliro a Swahaabah wina wake. Kenako adalankhula ndi ma swahaabah (radhiyallahu ‘anhum) omwe adalipo Ndipo adati: “Ndani mwa inu adzabwerera ku Madinah Munawwarah, ndipo paliponse akakawona fano kapena chiboliboli adzaziphwanya, ndipo paliponse pamene akaone mtumbira wa …
Read More »Allah Ta’ala Yekha Ndi Amene Amadyetsa Zolengedwa Zonse
Tsiku lina, m’nthawi ya Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) gulu la maswahaaba a fuko la Banu Al-Ash’ar lidayenda kuchokera ku Yemen kupita ku Madina Munawwarah ndi cholinga chopanga hijrah. Atafika ku mzinda odalitsika wa Madinah Munawwarah, adapeza kuti chakudya chawo chomwe adabwera nacho chatha. Choncho adaganiza zotumiza mmodzi mwa maswahaba awo …
Read More »Tafseer Ya Surah Faatihah
بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ ﴿١﴾ الْحَمْدُ لِلَّهِ رَبِّ الْعَالَمِينَ ﴿٢﴾ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ ﴿٣﴾ مَالِكِ يَوْمِ الدِّينِ ﴿٤﴾ إِيَّاكَ نَعْبُدُ وَإِيَّاكَ نَسْتَعِينُ ﴿٥﴾ اهْدِنَا الصِّرَاطَ الْمُسْتَقِيمَ ﴿٦﴾ صِرَاطَ الَّذِينَ أَنْعَمْتَ عَلَيْهِمْ غَيْرِ الْمَغْضُوبِ عَلَيْهِمْ وَلَا الضَّالِّينَ ﴿٧﴾ Kuyamikidwa konse ndi kwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse. Wachifundo Chambiri, Wachisoni. Mbuye wa tsiku lachiweruzo. Inu nokha timakupembedzanindipo kwa Inu nokha ndi kumene timakupemphani chithandizo. Tiwonetseni …
Read More »Chikhulupiliro Chokhazikika cha Ali (radhwiyallahu ‘anhu) pa Lonjezo la Allah Ta’ala
Zanenedwa kuti nthawi ina munthu wopempha adadza kwa Ali (radhwiyallahu ‘anhu) napempha kanthu. Ali (radhwiyallaahu ‘anhu) adatembenukira kwa mmodzi mwa ana ake awiri, Hasan kapena Husain (radhwiyallahu ‘anhuma), nati kwa iye: “Pita kwa amayi ako ukawawuze kuti ine ndati: “Ndidasunga dirham zisanu ndi imodzi. Ndipatseni Dirhamu imodzi mwa zisanu ndi …
Read More »