Daily Archives: June 10, 2026

Sunnati Ndi Adaab 2

6. Pangani ma dua komanso azkaar musanagone; اللَّهُمَّ بِاسْمِكَ أَمُوْتُ وَأَحْيٰ O, Allah Talaa mdzina Lanu ndikufa komanso ndiuka 7. Gonerani kumanja ndikuika dzanja lanu lamanja pansi pa tsaya lanu lakumanja. Bibi Hafsah (radiyallahu anha) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) akafuna kugona, ankaika dzanja lake lamanja pansi pa tsaya …

Read More »