Mtumiki (swallallahu ‘alayhi wasallam) adati, “Munthu amene amamwalira ndi mliri, amakhala wamwalira imfa ya shahid. Mu khilaafat ya Umar (radhwiyallahu ‘anhu), mliri wa Amwaas unakhudza Shaam m’chaka cha 17 pambuyo pa Hijrah. Mu mliriwu Abu Ubaidah (radhwiyallahu ‘anhu), mtsogoleri wa Asilamu ku Shaam, anakhudzidwa nawonso ndipo pambuyo pake anamwalira. Asanamwalire, …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu