admin

Chisangalalo cha Hazrat Umar (Radhiyallahu ‘anhu)

Olemekezeka Umar (Radhwiyallaahu ‘anhu) adanenapo nthawi ina kwa olemekezeka Abbaas (Radhwiyallahu ‘anhu) (amalume a Rasulullah (Swallallaahu ‘alayhi wasallam)) kuti: “Ndidakondwera ndi Chisilamu chanu kuposa Chisilamu cha abambo anga chifukwa Chisilamu chanu chidabweretsa chisangalaro chochuluka kwa Rasulullah swallallahu ‘alaihi wasallam) kuposa Chisilamu cha bambo anga. (Sharhu Ma’aanil Aathaar 3/321)

Read More »

Tafseer Ya Surah Nasr

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ إِذَا جَاءَ نَصْرُ اللَّهِ وَالْفَتْحُ ‎﴿١﴾‏ وَرَأَيْتَ النَّاسَ يَدْخُلُونَ فِي دِينِ اللَّهِ أَفْوَاجًا ‎﴿٢﴾‏ فَسَبِّحْ بِحَمْدِ رَبِّكَ وَاسْتَغْفِرْهُ ۚ إِنَّهُ كَانَ تَوَّابًا ‎﴿٣﴾‏ (Oh Muhammad (Swallallaahu ‘alayhi wasallam)) Kukadzafika chithandizo cha Allah Ta’ala ndi kupambana (kugonjetsa Makka Mukarramah) ndipo ukadzawaona anthu akulowa mu Dina ya Allah ali ambiri, choncho lemekeza ndi kutamanda Mbuye …

Read More »

Qa’dah ndi Salaam

1. Pambuyo pa sajda yachiwiri ya rakaah yachiwiri, khalani tawarruk kutanthauza kukhala ndi thako lakumanzere ndikutulutsa phazi lakumanzere pansi pa mwendo wakumanja. Phazi lakumanja likhale lowongoka ndi zala ziyang’ane kuchibla. Chidziwitso : Kukhala m’malo a tawarruk kumagwiranso ntchito pa swala yomwe ili ndi qa’dah imodzi mwachitsanzo rakaah ziwiri ndi qa’dah …

Read More »

Rakaah Yachiwiri

1. Mukamanyamuka pa sajdah, choyamba nyamulani chipumi ndi mphuno, kenako zikhato ndikumalizira mawondo. 2. Pamene mukuimirira Rakah yachiwiri, tsamizirani manja anu pansi uku mukuimilira.[1] 3. Pitirizani rakaah yachiwiri monga mwachizolowezi (kupatula Dua-ul Istiftaah simudzaiwerenga).[2] [1] وإذا أراد القيام من السجود أو الجلوس اعتمد بيديه معا على الأرض ونهض ولا أحب …

Read More »

jalsah

6. Iwerengeninso dua iyi pamene muli Pa Jalsah:[1] اللَّهُمَّ اغْفِرْ لِي، وَارْحَمْنِي، وَعَافِنِي، وَاجْبُرْنِي، وَارْفَعْنِي، وَاهْدِنِي، وَارْزُقْنِي Oh Allah, ndikhululukireni, ndichitireni chifundo, ndichotsereni kufooka kwanga, ndikwezeni pa udindo, ndiongolereni ndi kundidalitsa ndi riziki. 7. Nenani takbira ndipo pitirirani ku sajda yachiwiri monga mwachizolowezi.[2] 8. Imirirani kuchokera pa sajdah yachiwiri nkukhala …

Read More »

Hazrat Abu Bakr – manthu cha Ubwino ndi Chifundo

Tsiku lina Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adafunsa kwa ma Swahaabah (radhwiyallahu “anhum) kuti: “Ndani mwa inu amene akusala kudya lero?” Hazrat Abu Bakr (radhiyallahu anhu) adayankha: “Lero ndasala. Kenako Nabiy (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adafunsa. “Ndani mwa inu amene wayendera munthu wodwala lero?” Harrat Abu Bakr (radhiyallahu ‘anhu) adayankha: “Lero ndayendera …

Read More »

Sajdah

12. Werengani Takbiir ndikukhala pansi mukachoka pa Sajdah yoyamba, imeneyi imatchedwa kuti I’tidaal.[1] Jalsah 1. Mukukhala kwanu pa jalsah, ikani manja anu pa ntchafu zanu ndi zala zanu pafupi ndi mawondo anu.[2] 2. Gwirizanitsani zala zanu.[3] 3. Yang’anani malo a Sajdah uku muli pa Jalsah.[4] 4. Phazi lakumanja likhale lolunjika …

Read More »

Munthu Woyamba wa Ummah uwu kukalowa ku Jannah

M’ Hadith ya yodaliysika, Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adalongosora kuti Ummah wake udzalowa ku Jannah pamaso pa ma Ummah ena onse, ndipo kuchokera mu Ummah wake wonse, Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adzakhala munthu woyamba kulowa ku Jannah pambuyo pake. Mtumiki (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adati: “Hazrat Jibreel (‘alaihis salaam) adaonekera …

Read More »

Ubwino Waukulu Wowerenga Durood Tsiku la Jumuah

عن أوس بن أوس قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: إن من أفضل أيامكم يوم الجمعة فيه خلق آدم وفيه قبض وفيه النفخة وفيه الصعقة فأكثروا علي من الصلاة فيه فإن صلاتكم معروضة علي قال: قالوا: يا رسول الله وكيف تعرض صلاتنا عليك وقد أرمت يقولون بليت فقال: …

Read More »