admin

Kumuzindikiritsa Mwana Kwa Allah

Kulera mwana n’kofunika kwambiri ndipo tingakuyerekezere ndi maziko a nyumba. Ngati maziko a nyumba ali olimba, ndiye kuti nyumbayo idzakhalanso yolimba ndipo idzapirira ku nyengo iliyonse. Mosiyana ndi zimenezi, ngati maziko a nyumbayo ndi ofooka komanso ogwedezekagwedezeka, ndiye kuti ndi kugwedezeka pang’ono, nyumbayo idzagwa. Chimodzimodzinso, kulera mwana ndiko maziko amene …

Read More »

Kutonthoza Oferedwa

7. Nkoloredwa kuyamikira omwalirayo. Komabe, pomutamanda, onetsetsani kuti simukukokomeza kapena kumutamanda pa makharidwe amene panalibe mwa iye. Momwemonso musatengere chikharidwe ndi njira za makafiri pomutamanda. 8. kuchuluka kwa nthawi ya ta’ziyat ndi masiku atatu kuchokera tsiku lomwalira. Pambuyo pa tsiku lachitatu, ndi makruh kupanga ta’ziyat. Komabe, ngati munthu sadathe kubwera …

Read More »

Ma Sunnah Komanso Miyambo Yochezera Ndi Namfedwa

1. Ta’ziat imatanthauza kugawana chisoni ndi ananfedwa ndi kuwamvera chisoni pa kutaika kwa okondedwa wawo. Izi zimachitika pomupangira dua omwalirayo pamaso pa akubanja ake. Momwemonso izi zidzachitika polipangira Dua banja lake, kupempha Allah Odalitsika ndi Wapamwambamwamba, kuti awadalitse powapatsa kupilira ku mayesero amenewa. 2. Dua ingachitike m’mawu awa: “Allah amupatse …

Read More »

Dua ya Hazrat Said bin Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu) Iyankhidwa

Nthawi ina, Arwa bint Uwais, neba wa Hazrat Said bin Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu), adadza kwa Muhammad bin ‘Amr bin Hazm (Rahimahullah) ndi dandaulo lokhudza neba wake Hazrat Sa’eed bun Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu). Ananena kuti adamanga khoma lake m’malo mwake ndipo adapempha Muhammad bin Amr (Rahimahullah) kuti apite kwa iye kuti …

Read More »

Kutonthoza Oferedwa

Chisilamu ndi njira yokwanira komanso yangwiro ya moyo yomwe yaganizira zosowa zonse za munthu. Sizinangosonyeza njira ya mtendere m’moyo wa munthu, komanso zasonyeza mmene tingasonyezere chikondi ndi mtendere munthu akamwalira. Choncho Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adausonyezera Ummah momwe ungatonthozere ndi kuwapepesa ofedwa amene ali m’masautso. Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adati: …

Read More »

Sayyiduna Sa’iid Ibn Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu) Ayikidwa m’gulu la Otenga nawo gawo pa nkhondo ya Badr

Nkhondo ya Badr isanayambike, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) atamva kuti gulu la ochita malonda la Ma Quraish, lolemedwa ndi chuma chawo, lachoka ku Shaam (Syria) ndipo likubwerera ku Makkah Mukarramah, adatumiza Talhah bin Ubaidullah ndi Sa’iid radhwiyallahu anhuma kuti akasonkhanitse uthenga okhudza Gululi. Izi zidachitika masiku khumi Rasulullah (Swalla …

Read More »

Maduwa Oyenera Kupanga Ukakamuona Odwala

Dua Yoyamba لا يَأْسَ طَهُورٌ إِنْ شَاءَ الله Palibe chifukwa chodera nkhawa, insha-Allah kudzera m’matendawa, muyeretsedwa. (i.e. Palibenso chifukwa chilichonse choti mude nkhawa kapena kuchita mantha. Mukungoyeretsedwa ku Uzimu, mukuyeretsedwa ku machimo anu, ndipo kuthupi, thupi lanu likuyeretsedwa ku poizoni. Choncho, pamene matenda abwera kwa inu ngati chifundo chobisika kumbali …

Read More »

Hazrat Abdur Rahmaan bin Auf (Radhiyallahu ‘anhu) Kusamalira akazi olemekezeka a Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) paulendo wa Hajj

Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) adati: “Ndithu, amene angadzasamalire akazi anga ndikadzamwalira, ndiye munthu owona ndi owopa Allah. Atamwalira Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam), Olemekezeka Abdur Rahmaan bun Auf (Radhwiyallahu ‘anhu) ankakhala myandikana ndi Azwaaj Mutahharaat (akazi olemekezeka a Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam)). …

Read More »

Ana Olungama – Cholowa Cha Tsiku Lachiweluzo

Zina mwa zabwino zamtengo wapatali za Allah pa munthu ndi mdalitso okhala ndi ana. Mdalitso okhala ndi ana ndi ena mwa Ni’ma yapadera ya Allah, zomwe zatchuridwa mu Quraan Majiid. Allah  Akunena: وَاللَّهُ جَعَلَ لَكُم مِّنْ أَنفُسِكُمْ أَزْوَاجًا وَجَعَلَ لَكُم مِّنْ أَزْوَاجِكُم بَنِينَ وَحَفَدَةً وَرَزَقَكُم مِّنَ الطَّيِّبَاتِ Allah adakulengerani akazi …

Read More »

Ma Sunnah Komanso Miyambo Yokaonera Odwala 2

4. Mukamayendera odwala, pemphani dua iyi: لا بَأْسَ طَهُورٌ إِنْ شَاءَ اللهُ Palibe chifukwa chodera nkhawa, insha-Allah kudzera mu matendawa, muyeretsedwa. Mukhozanso kubwereza dua iyi kasanu ndi kawiri: أَسْأَلُ اللهَ الْعَظِيمَ رَبَّ الْعَرْشِ الْعَظِيمِ أَنْ يُشْفِيكَ Ndikumupempha Allah Wamphamvu zoposa, Mbuye wa Mpando Wachifumu waukulu, kuti akuchizeni. عن ابن عباس …

Read More »