Mantha a Hazrat Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) kuliopa tsiku lachiweruzo

Sayyiduna Haani (rahimahullah), kapolo womasulidwa wa Sayyiduna “Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu), akunena kuti: Hazrat ‘Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) ankati akayima pamanda, ankalira kwambiri moti ndevu zake zinkanyowa ndi misozi yake. Wina adamufunsa kuti: “Timakuwona kuti ukakumbukira Jannah ndi Jahanmum kapena kukambidwa  za izo, siumakhudzidwa kwambiri mpaka kuyamba kulira, pomwe ukayima pamanda timakuona …

Read More »

Jalsah

1. Nenani takbira ndipo khalani tsonga (jalsah). 2. Phazi lakumanja muliyimike ndi zala zake ndikuyang’anitsa ku qibla. phazi lakumanzere muligoneke ndikulikhalira. 3. Khalani mokumanitsa ntchafu zanu pamodzi (muzikumanitse). 4. Ikani manja anu pa ntchafu ndi zala pamodzi ndipo nsonga za zala zanu zikhale m’mphepete mwa mawondo. 5. Yang’anani malo omwe …

Read More »

Kutsatira Njira Yofewa ndi Yodekha Pochita zinthu ndi Anthu:

“Ataa bin Farrookh (rahimahullah) akufotokoza motere: Tsiku lina lake ‘Uthmaan (radhwiyallaahu ‘anhu) adagula malo kwa munthu wina. Atagula malowa ‘Uthmaan (radhwiyallahu ‘anhu) adadikira kuti munthuyo adzatenge ndalama zake. Komabe, munthuyo sanabwere. ‘Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) adakumana ndi munthuyo pambuyo pake ndipo adamufunsa: “Bwanji sunabwere kudzatenga ndalama zako?” Bamboyo anayankha. “Chomwe chinandipangitsa …

Read More »

Tafseer Ya Surah Falaq Ndi Surah Naas

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ أَعُوذُ بِرَبِّ الْفَلَقِ ‎﴿١﴾‏ مِن شَرِّ مَا خَلَقَ ‎﴿٢﴾‏ وَمِن شَرِّ غَاسِقٍ إِذَا وَقَبَ ‎﴿٣﴾‏ وَمِن شَرِّ النَّفَّاثَاتِ فِي الْعُقَدِ ‎﴿٤﴾‏ وَمِن شَرِّ حَاسِدٍ إِذَا حَسَدَ ‎﴿٥﴾‏ Nena (iwe Muhammad (Swallallaahu ‘alayhi wasallam): “Ndikudzitchinjiriza mwa Mbuye wa m’bandakucha, ku zoipa zonse zomwe Adazilenga, ndi ku zoipa za mumdima (wa usiku) pamene mdima wake ukufalikira; …

Read More »

Sajdah

1. Nenani takbira ndikupita pa sajdah. 2. Gwirani manja anu m’mawondo pamene mukupita pa sajdah 3. Choyamba ikani mawondo pansi, kenako zikhatho, ndipo pomalizira pake chipumi ndi mphuno pamodzi. 4. Siyani zala zotsekeka moyang’anitsa ku chibla. 5. Ikani zikhatho zanu pansi m’njira yoti zala zifanane ndi makutu ndipo mbali zigwirizane …

Read More »

Hayaa ya Hazrat ‘Uthmaan (Radhiyallahu ‘anhu)

Hazrat Aaishah (radhiya allahu ‘anha) akusimba motere: Nthawi ina, Mtumiki (swalla allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) anali atagona kunyumba kwanga ndipo thupi lake linasunthidwa pang’ono kuchokera kudera la ntchafu zake zodalitsika kapena ntchafu yake yodalitsika, ngakhale ntchafu zodalitsidwa ndi shins zidakutidwa ndi lungi lake. Panthawi imeneyo, Abu Bakr (radhiyallahu ‘anhu) …

Read More »

Ruku ndi I’tidaal

6. Timisomali tamapazi onse awiri akhale pamodzi. Ngati izi ndizovuta, ndiye kuti ziyenera kusungidwa moyandikana momwe zingathekere(momwe mungakwanitsire). 7. Yang’anani malo a sajdah m’maimidwe a ruku (pamene muli pa ruku). 8. Werengani tasbeeh katatu kapena nambala ina iliyonse yosagawika pawiri.   سُبْحَانَ رَبِّيَ الْعَظِيْم Subhaana rabbiyal A’dhwiim Kuyeretsedwa konse ndi …

Read More »

Nkhani Zabwino Za Jannah

Sayyiduna Abu Muusa (Radhwiya Allaahu ‘anhu) akufotokoza motere: Tsiku lina ndidali limodzi ndiMtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) mu umodzi mwa minda ya zipatso zaku Madinah Munawwarah pamene munthu wina adadza napempha chilorezo cholowa m’mundawu, atamva pempho la munthuyo, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) anandiuza. “Mlole alowe ndikumuwuza nkhani yabwino yokhala …

Read More »

Ruku ndi I’tidaal

1. Mukamaliza kuwerenga Surah Faatihah ndi surah ina, yimani kaye pang’ono ndipo pambuyo pake kwezani manja (monga momwe tafotokozera mu takbeeratul ihraam) uku mukunena takbira ndikupita pa rukuu. Zindikirani: Takbeeraat intiqaaliyyah (takbeer yomwe imanenedwa posuntha kuchoka ku kaimidwe kena kupita ku kena) iyenera kuyambika munthu akangoyamba kusuntha kupita ku kaimidwe …

Read More »

Msilamu Woyamba Kuchita Hijrah (kusamuka) ndi Banja Lake

Olemekezeka Anas (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Uthmaan (radhwiyallahu anhu) adanyamuka kupita ku Abyssinia, kusamuka ndi mkazi wake olemekezeka, Bibi Ruqayyah (radhwiyallahu anha), mwana wamkazi wodalitsika wa Rasulullah (swallallaahu alaih wasallam). Nkhani zokhudza momwe amakhalira zidachedwa, choncho Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adali ndi nkhawa ndipo amatuluka ku Makka Mukarramah kufuna kudziwa …

Read More »