Munthu Woyamba wa Ummah uwu kukalowa ku Jannah

M’ Hadith ya yodaliysika, Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adalongosora kuti Ummah wake udzalowa ku Jannah pamaso pa ma Ummah ena onse, ndipo kuchokera mu Ummah wake wonse, Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adzakhala munthu woyamba kulowa ku Jannah pambuyo pake. Mtumiki (swallallaahu ‘alayhi wasallam) adati: “Hazrat Jibreel (‘alaihis salaam) adaonekera …

Read More »

Ubwino Waukulu Wowerenga Durood Tsiku la Jumuah

عن أوس بن أوس قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: إن من أفضل أيامكم يوم الجمعة فيه خلق آدم وفيه قبض وفيه النفخة وفيه الصعقة فأكثروا علي من الصلاة فيه فإن صلاتكم معروضة علي قال: قالوا: يا رسول الله وكيف تعرض صلاتنا عليك وقد أرمت يقولون بليت فقال: …

Read More »

Sajdah

7. Asungeni manja anu M’mbali.[1] 8. Yang’anani pa malo a Sajdah.[2] 9. Sungani mpata pakati pa mimba ndi ntchafu.[3] 10. Miyendo yonse iwiri ikhale pansi ndi zala zammiyendo zitaloza ku chibla. Sungani mpata wa dzanja limodzi pakati pa mapazi anu pa sajdah.[4] 11. Werengani katatu kapena nambala yosagawika ndi 2 …

Read More »

Hazrat Abu Bakr (Radhwiyallahu ‘anhu) akhala Wokonzeka kupereka nsembe ya china Chilichonse

Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wa sallam) Pankhondo ya Badr, mwana wa Abu Bakr Siddeeq (radhwiyallahu anhu) Hazrat Abdur Rahmaan (Radhwiyallahu ‘anhu), anamenya nawo mbali ya okanira poti iye adali asadakhulupirirebe Chisilamu. Pambuyo pake, atalowa Chisilamu, ali chikhalire pansi ndi bambo ake, Hazrat Abu Bakr Siddeeq (Radhwiyallahu “anhu), adati: “E, inu abambo …

Read More »

Tafseer Ya Surah Kaafiroon

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ يَا أَيُّهَا الْكَافِرُونَ ‎﴿١﴾‏ لَا أَعْبُدُ مَا تَعْبُدُونَ ‎﴿٢﴾‏ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ‎﴿٣﴾‏ وَلَا أَنَا عَابِدٌ مَّا عَبَدتُّمْ ‎﴿٤﴾‏ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ‎﴿٥﴾‏ لَكُمْ دِينُكُمْ وَلِيَ دِينِ ‎﴿٦﴾‏ Nena: “E, inu anthu osakhulupirira! Ine sindingapembedze (mafano) amene mukuwapembedza, ndiponso simum’pembedza Amene ine ndikum’pembedza (Allah Ta’ala). Ndipo inu simunhampembedze (Allah) Amene ine ndikumupembedza …

Read More »

Sajdah

1. Nenani takbira, ndipo popanda kukweza manja anu, pitani pa sajdah.[1] 2. Gwirani manja m’maondo uku mukupita pa Sajdah.[2] 3. Yambani ndikuika mawondo pansi, kenako manja, ndipo pomalizira pake Ikani chipumi ndi mphuno pamodzi.[3] 4. Ikani zikhatho pansi m’njira yoti zala zifanane ndi makutu ndipo mbali zapansi zigwirizane ndi mapewa.[4] …

Read More »

Chikondi cha Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) Kugwirizana ndi Chikondi cha Rasulullah (Sallallahu ‘alaihi wasallam)

Bambo ake a Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) atalowa Chisilamu. Hazrat Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adalankhula kwa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) kuti: “Ndikulumbirira amene anakuikani m’choonadi! Ngakhale ndiri mchisangalaro kuti bambo anga alowa chisilamu, ndikadakhala osangalala kwambiri zikanakhala kuti omwe alowa chisilamu ndi amalume anu Abu …

Read More »

Olemekezeka Abu Bakr (Radhwiyallahu ‘anhu) amutumikira Rasulullah (Swallallaahu ‘alayhi wasallam)

Hazrat Abu Bakr Siddeeq (Radhwiyallaahu ‘anhu) akusimba motere za ulendo wa Hijrah ndi Rasulullah (Swallallaahu ‘alayhi wasallam): Tinayenda mofulumira usiku wonse ndi gawo lina la tsiku lotsatira mpaka kutentha kwamasana kunakula kwambiri. Kenako ndinapeza kuti mseu mulibe munthu aliyense woyendamo. Ndinayang’ana kutsogolo kuti ndione ngati ndingapeze mthunzi uliwonse kuti tibisalemo. …

Read More »

Ruku Ndi I’tidaal

6. Onetsetsani kuti manja asungidwa kutali ndi thupi.[1] 7. Lankhulani katatu kapena nambala yosagawanikana.[2] سُبْحَانَ رَبِّيَ الْعَظِيمِ Walemekezeka Mbuye wanga, Wamkulukulu. 8. Pambuyo powerenga tasbeeh, imirirani kuchokera ku rukuu uku mukunena tasmee:[3] سَمِعَ اللهُ لِمَنْ حَمِدَهُ Mulungu amamva amene Wamtamanda. 9.Kwezani manja (monga momwe tafotokozera mu takbeeratul ihraam) ndipo ikani …

Read More »

Ulemu wa Hazrat Abu Bakr (Radhiyallahu ‘anhu) kwa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wasallam) ndi chikondi cha Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) pa Iye

Pa nthawi ya Fat-he-Makkah Mukarramah (Kugonjetsa Makka Mukarramah), Hazrat Abu Bakr (Radhwiyallahu ‘anhu) adabweretsa bambo ake, Abu Quhaafah, kwa Rasulullah kuti akalowe Chisilamu. Pa nthawiyo Abu Quhaafah adali ndi zaka zoposa 90 zakubadwa ndipo adali atasiya kuona. Atadza kwa Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wasallam), Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wasallam) adamuuza Hazrat Abu …

Read More »