Sunna Za Msikiti

37. Ulumikizitseni mtima wanu nthawi zonse ndiku mzikiti. Mwachitsanzo pamene mukuchoka mumzikiti pomwe mwatsiriza swalah yanu, pangani niya kuti mubweranso kumzikitiko paswala yotsatirayo ndipo idikireni swalayo ndimtima onse.[1] عن أبي هريرة رضي الله عنه أن رسول الله صلى الله عليه وسلم قال ألا أدلكم على ما يمحو الله به الخطايا …

Read More »

Chikondi chomwe Zaid bin Dhathinah (radhiyallahu anhu) ankamuonetsera Mtumiki (sallallahu alaih wasallam)

Makafiri ali pafupi kuti amuphe sahabah Olemekezeka Zaid bin Dhathinah (radhiyallahu anhu) adamufunsa kuti ungasangalale kuti m’malo mwako timuphe Muhammad ndikuti iweyo tikusiye udzikasangalala ndi banja lako? Yankho lake lodabwitsa lidali loti ndikulumbira mwa Allah sindingalore kuti ine ndikhale ndi banja langa kumasangalala ndipo Muhammad akuvutika ngakhale kutakhala kubaidwa ndi …

Read More »

Machimo a Zaka Makumi asanu ndi atatu Akhululukidwa, sawabu za Zaka Makumi asanu ndi atatu Zilembedwa Kupyolera mu Kubwereza Durood Makumi asanu ndi atatu tsiku Lachisanu.

وعن سهل بن عبد الله قال من قال في يوم الجمعة بعد العصر اللهم صل على محمد النبي الأمي وعلى إله وسلم ثمانين مرة غفرت له ذنوب ثمانين عاماً أخرجه ابن بشكوال وقد تقدم قريباً في حديث أبي هريرة معناه (القول البديع صـ 400) Zidanenedwa ndi Hazrat Sahl bun Abdullah …

Read More »

Sunna Za Msikiti

34. Kutha kwa Adhana, ngati sudapemphere swalah, usatuluke mumzikiti pokhapokha patakhala zifukwa zomveka bwino.[1] عن أبي الشعثاء قال كنا قعودا في المسجد مع أبي هريرة رضي الله عنه فأذن المؤذن فقام رجل من المسجد يمشي فأتبعه أبو هريرة رضي الله عنه بصره حتى خرج من المسجد فقال أبو هريرة رضي …

Read More »

Sayyiduna Abu Ubaidah (radhiyallahu) anhu aluza mano ake

Pankhondo ya Uhud Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adavulazidwa kwambiri ndi adani ndipo zitsulo za chipewa chake chodzitetezera pa nkhondo zinabaya pankhope yake yolemekezeka. Sayyiduna Abu Bakr Siddiq komanso Abu Ubaidah (Radhiyallahu anhuma) adathamangira kukamuthandizira Rasulullah (sallallahu alaih wasallam). Sayyiduna abu Ubaidah (radhiyallahu anhu) atafika pamene panali Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) …

Read More »

Tafseer Ya Surah Humazah

Tsoka kwa aliyense ochita miseche, wonyoza, wodziunjikira chuma ndikuchiwerengera! Akuganiza kuti chuma chake chidzamkhazika muyaya. Ayi! Ndithu, adzaponyedwa ku Hutwamah (kumoto waukali). Ndipo nchiyani chingakudziwitse kuti 'Hutamah' ndi chiyani? Ndi moto wa Allah woyatsidwa umene uzidzalowa m’mitima mwawo. (Motowo) udzatchingidwa ndi zipupa zitalizitali, ndi mizati yotambasulidwa (yotambasuka).

Read More »

Masunnah Ochita Mumzikiti

31.  Kupatula kupita kumzikiti kukapemphera, ngati kuli mtsonkhano omwe ukupangidwira mumzikiti, mukuyenera kupanga niya kuti mukupita kumzikiti kukaphunzira za Dini. Ngati wina angakwanitse kuphunzitsa dini choncho akuyenera kupanga niya kuti akubwera kumzikiti kukaphunzitsa dini. عن أبي هريرة رضي الله عنه قال سمعت رسول الله صلى الله عليه وسلم يقول من …

Read More »

Machimo a zaka 80 akhululukidwa, kulandira malipiro ochita ibaadah kwa zaka 80 kudzera mu kuwerenga Duruud

Hazrat Abu Hurairah (radhwiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki sallallahu (sallallahu alaih wasallam) adati: munthu amene angaswali Asr tsiku la Jumuah ndipo kenako ndikuyamba kuwerenga Duruud iyi kokwana ka 80 asadaimilire malo wakhalawo, amakhululukidwa machimo a zaka 80 ndiponso amalipidwa zabwino kukhala ngati wapanga ibaadah kwa zaka 80.

Read More »

Masunnah Ochita Mumzikiti

27. Khalani mwaulemu ndi modekha pamene muli mumzikiti musakhale moiwala kulemekezeka kwa mzikiti. Anthu ena pamene akudikilira swalah kuti ichitike amaseweretsa zovala zawo kapena kusoweretsa mafoni. Kumeneku ndikuphwanya kulemekezeka ndi ulemelero wa mnzikiti.[1] 28. Thandizirani poupanga mzikiti kuti ukhale waukhondo nthawi zonse.[2] عن أبي سعيد الخدري رضي الله عنه قال …

Read More »